Email a copy of 'Catholic Parish in Hewe named after courageous Bishop Zuza of ‘Chindere chakufikapo’ rap' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Catholic Parish in Hewe named after courageous Bishop Zuza of ‘Chindere chakufikapo’ rap' to a friend
The Pentecostal Life Church International (PLCI) has organised a two day healing and deliverance crusade which will take place on...
Mr Dulani says since the bishop critcised Bingu at Comesa the popularity of the party and its leadership went down dramatically. How did you measure it? I thought you would measure his popularity by looking at what people said in the 2014 elections? Akulu inu mukukhalanso ngati simunapite ku school. M’mayesa ndinu mumapanga za Afrobarometer nkumatiuza kuti DPP is ahead of other parties and might win the elections? MCP inakulowani m’magazi akulu inu.
Nkhani ya madzi yomweyi mwapweka nayo? Shooting yourself on the foot. I saw Chakwera in Parliament making chibwibwi on the issue. Anawa muziwalanga.
But ife a dpp we have been outshined. A major catholic event being graced by opposition. A Dausi mutipo chani apa? Boma talandilidwatu apa.
Mpaka ngongole zomwezi? this Government is indeed Broke
Nanunso a chakwera mabvuto anu ndi angati? Mukukathandiza mpingo ooti ndi olemera ndikale. Ndani amene asakudziwa kuti mpingo wakatolika ndiolemera? Umakhala ukuchita criticize boma munjira zambiri. Kodi iwe ukanakhala oti ndalama wapatsa a katolikayo, wakapereka kuchipatala olo kudera lakwanu kuti achite kachitukuko kena, sukanalemekezeka? Kodi iwe chiyambireni chomwe wapanga kudera lakwanu cholodzeka ndi chiyani? Akatolika omwewo ndi amene anapangitsa kuti MCP ichoke m’boma, ukuganiza kuwapatsa ndalama pano ndiye akuthandizira kuti MCP ibwelere m’boma? Walemba mmadzi aise.
Indeed it has to be St Joseph Mukasa of Uganda because Bishop Joseph Mukasa Zuza is not yet a Saint!!
Mukukanganilira mpingo chifukwa cha mavoti, ng’o!
St Joseph Mukasa of Uganda (one of the Martyrs of Uganda)! Zuza got his name after the Ugandan martyr
K5million kwacha and K2million zaziiii osapereka bwanji summadziwa za izi.
Koma inu mukuona ngati oChakwera wo ndo oMia wo kumpotoko angapezeke kanthu ndi mmene akutimbila atumbukamu?
Santana , you comments on issues blindly since u are acadent boy, can you compare , how pipo voted for DPP in 2009 and 2014 that difference is what Mr Dulani mean, so pliz don’t just comment for the sake of publicity