Email a copy of 'Catholic University of Malawi students suspected of murder after pub row' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Catholic University of Malawi students suspected of murder after pub row' to a friend
Malawi Communications Regulatory Authority (Macra) has formally issued out a 10 year licence to mobile telecommunication service provider Lacell Private...
Level yamaphunziro anu anthuni ku University ndiya utsogoleri mukakayamba zintchito tsano muyenera kumazolowera kukhala ndi anthu and tazionetsani kuti ink yambiri yili ndi zipatso zabwino ndithu.Pena ndikumadabwanso zikuchika mudziko la Malawi palikusiyana kwakulu zedi ndi maiko ambiri becoz masiku ano you know we have televisions tikuphunzira ndi kusirira ubwino wa anthu ophunzira bwino.The more anthu akamaphunzira dziko lima kwera miyoyo ya anthu koma with Malawi its opposite,kalero kuli anthu ochepa ophunzira this country was wonderful pomwe lero ink zambiri koma useless ndipo muzimvere chisoni nonse you are doing nothing than kuononga dziko sitikudabwa nanu ayi.Kuphunzira kwaku Malawi ndikomweko if you… Read more »
Akapitiliza tibweza chipogwe cause kaya munthuyo analakwisa koma tikuyng’ana kuti wataya moyo cause of kumenyedwa ndi maduka ndikukamutaya pafupi ndi nyumba za FIC
Mutipeze kuno Ku Chanco…ana osasamba inu . Kulimbana ndi ma pelli basi
mmm zovuta..munthu uyu amakamila ndeu uyu..I was there…RIP
I do not know if the law will be applied to them,being some of them,nephews and nices of bishops,priests and sisters. Let us wait and see!!!!!!!!!!!!
Ana akusukulu ya Ukachenjede ya Katolika (UkaKato) hei! Izi olo ife amene tili ku University yeni yeni (UNIMA) bambo,sitipangepo! Ife timangophuzula ndikugawa mimba mwaChikandamu koma sitipha! Silly stupid ana opanda nzeru nchifukwa chake simuli ku University yeni yeni !!!
NAGULU A CHINA MPHWIYO NDI KASAMBALA AMENEWO
ZIGAWENGA ZA MA DEGREE AWO
NDI MAPOLOFESA
MUNTHU WAMBA SIMUYESA MUNTHU !!
The problem is not the location of the college. In fact being in the rural setting would mean a conducive environment for study, away from the hustle and bustle of urban activity. I have been to this college and noticed how students guzzle, and are generally unruly. As others have commented, this is a capital offence. Let the law take its course
wasted generation
catholic university must just build a common room so that students must drink there and relax koma kumamwa mowa ndi anthu ammuzi mapeko ake amakhala amenewa a student ndimunthu wovuta kumumvesa!