Email a copy of 'CCAP Livingstonia Synod rejects meeting Ngoni chiefs on polygamy, booze' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

13 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
bwanaloli
5 years ago

Rt. Reverand Levi Nyondo is very right. why should the church accept your stupid and weaked ngoni culture. what is so special with women and beer? . weakness can never be tolerated in church. You’re free to join other churches if you want but which church can accept the ngoni’s? . It is very shameful to hear from the paramount chief advocating for stupidity instead of warning his subjects regarding the HIV pandemic.

drogba
5 years ago

Nyondo simtumbika ndi Lambia ku Chitipa

Ndadabwa
5 years ago

bravo bambo Nyondo. I agree with you no compromise over Bible teaching

Hewe
Hewe
5 years ago

Atsikana koma a chilhomwe. Awa mbina njeeee and maujeni osakoka. Wamkulu wamng’ono chimodzimodzi? Shaaaah.

Nyondolosi
5 years ago

Levi awiske mba mitala. He should start from condemning his father…demeti.

Ise as ngonis will protect and uphold our cultural heritage and values. Timwenge mowa nakutola wanakazi naumo takhumbira.

Nyondolosi
5 years ago

Levi awiske mba mitala. Wakayambe na awiske. Not us the ngonis

Baza
Baza
5 years ago

WAYETHE NKOSI,
Phuma uhambe Livingstonia Synod. Matchalichi nganandi (Chipangano, Apostole, Zion olo Islam!)
Ise timwenge nakutola wanakazi umo tikukhumbila. Nyondo iwe tilekele mdauko withu. Iwe Chiuta uli kuyowoyapo nayo kuti wakuphalire kuti mowa na mitala nkhwananga? Davide mbu? Solomon Ke?

Vyako ivo Nyondo.

LEGO
5 years ago
Reply to  Baza

Mulive nzeru,inu mukuona ngati nde udolo?

Zam'tonda
Zam'tonda
5 years ago

Siyahlupheka thina abangoni asim’boni Uthixo sithanda izintombi maningi now that Robert Laws deliberately wooed these warrior people into church times are not in the tracks of Laws the Ngoni must move with times that’s more reason why Mzimba is in development stagnation the Mbelwa house has any vision for Mzimba people we are graceful to God for Levi Nyondo for telling them the simple truth. The Anglican church broke away from the papacy it’s obvious that King Henry in his time was advancing his personal agenda today the Anglican church doesn’t entertain polygamy due to its internal evolution after all… Read more »

amdala bambo
amdala bambo
5 years ago

The Bible says: Anthu onse akhale abodza koma Mulungu yekha akhale olungama . We are in the last days anthu kumachita kukakamira uchimo motero . Baibulo lilizasintha kuzofuna zanu sizizatheka anta mpang’ono pomwe. Chibvumbulutso akunena kuti oipa akhalebe chiyipile , oledzera akhalebe chiledzelere, hule akhalebe hule, otamba akhalebe chitambire , olungama akhalebe olungama. Chisankho chilindi wina aliyense payekhapayekha. ulendowu ndiwayekhawayekha ndipo aliyense akaima pampando wachifumu wakuweruza , chimene munthu akufesa ndichimene azatute . Dziwani ndinu wolengedwa obey the creator and His word.

Hunga
Hunga
5 years ago
Reply to  amdala bambo

Kodi Livingstonia ndiye yoyera eti? Si mwe aja adakanika kulolerana ndi Nkhoma Synod pa za malire aja.? Always atumbuka atumbuka. What a bigger than size tribe?

Mbenawa
Mbenawa
5 years ago
Reply to  Hunga

Join the discussion

Mbenawa
Mbenawa
5 years ago
Reply to  Hunga

Nkhumuonga Chiuta chifukwa chakutipa Rev. Dr. Levi Nyondo, a minister who always speaks the truth, unenesko ngwakuti kwananga nkhwananga ndipo chi khristu kaya Chisilamu sichitengera mtundu or one’s culture. Ngata wasankha kukhala mu Khristu or Musilamu, you need to abide by the provisions of these doctrines. Angoni mowa ndi mitala ndichikhalidwe chawo inde, koma iwo amene ali a Khristu enieni ayenera kuzisiya izi. Abusa a Nyondo muli ndi mwai mukunyozedwa Kamba kolalikira choonadi posaona status yamunthu. Kunena zoona kunja kwaopsya uku, ndiye Mafumu ena adzilimbikitsa mitala – uuummm! zikundiopsya izi atsogoleri Ngati makolo a Rev. Nyondo ndi amitala, we thank… Read more »

Read previous post:
Cockpit hosts an All Black Party tonight- Farewell to the Princesses, in support of Fund a Girl Initiative

The famous VVIP night club, Cockpit Lounge, will tonight, host an all-black themed party to bid farewell to the Lilongwe...

Close