Email a copy of 'Chakwera as an MP has right to ask questions - Speaker' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chakwera as an MP has right to ask questions - Speaker' to a friend
Malawi's 193 strong member National Assembly on Thursday unanimously passed a motion to allow government disburse for utilization all budgetary...
The man has now realized kuti uphungu (u MP) ndiye saizi yake osati upulezidenti. Upulezidenti ndi wa ma big ngati achina APM. Kunsaila wamupatsa mkuluyi pressure mpaka kukumbuka ntchito za MP. A Chakwera kubwera ndiye kumeneko osati zochita mademo posapota zoti amuna azikwatirana amuna okhaokha kumuthandizira Trapence.
Uyu athera pa u emupi pomwepa. Can never rule Malawi
Ndendeuli, ukanakhala kuti umawinitsa anthu ndi iweyo komanso kuti Mulungu ndi mbale wako ndikanavomereza zomwe wanenazo. Koma poti suli zonsezi ingokhalani chete.
Failed Reverend cum politician wanting development in his area? Ndimayesa mumungokhalira kutsutsa paja. Lero mwavomereza kuti 4 billion igawidwe ku ma constituency anu mwaona nthawi yatha. Mwaiwala mwezi wazana munali pa nseu ndi ma CSO kukana same money. Hypocricy
What are you saying you DPP supporter? za zii zopanda park zopanda Mchere! What is wrong with asking for development project?
Umbuli siwabwino. Mukuonetsatu umbuli bwana mulopwana apa. Anakuuzani ndani kuti munthu wa Mulungu sayenera kutumikira dziko kapena anthu?
His Excellency the state president 2019 May 22 has asked the question.