Email a copy of 'Chakwera blocked from giving eulogies at Mpasu’s funeral' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

43 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
hatton
hatton
6 years ago

Abale a kongilesi kukonda kusokoneza maliro a eni ake. Zomwe amafuna kuchita a Chakwera zandikumbutsa zomwe anachita a Tembo and anzao kumaliro a amfumu ena ku Lilongwe zaka za mbuyomu.
Nthawi yomwe malemu Mpasu anali MP komanso Speaker nkuti a Chakwera akugwetsa mpingo wa Assemblies of God ndi ulamuliro wao woipa zedi.
mkuluyu popeza ndiwolimbira kulankhula m’maliro tingomulola azilankhula m’maliro a azibusa. Komanso tikudabwa chifukwa chomwe mkuluyu sanapemphe kuti alankhule pa mwamboo wa maliro a Bishop Kanyama (mzimu wao uwutse ndi mtendere)?
Kodi Mkakayu akulankhula ngati ndani? is that not contempt of court that reinstated all the previous NEC members?

santana
santana
6 years ago

Kodi eni mbumba ndiwomwe analamula kuti maliro ayikidwe ndi asilikari? Eni mbumbawo anali wokondwa kuti m’bale wawo waikidwa ndimwambo wa boma. The VP was enough to speak on behalf of Malawians. Chilima was not speaking as a DPP member but on behalf of the First Man on the land of Malawi. Chakwera would have spoken on behalf of Mpasu if he died as an MP. But still it was the Speaker to speak on such a funeral not Chakwera. Let him stick himself to party issues. He is not GOVT but this funeral was in the hands of govt. He… Read more »

Nyasi mmawso
Nyasi mmawso
6 years ago

Mudziwe kuti pa Maliro mphavu zimakhala ndi eni mhumba kapena mtundu kupanga madongosolo. Koma poti dzikoli tinapeleka kwa athakati oti chilichonse amayikapo ndale thats why zimakhala choncho. Dziko likufunika anthu odziwa miyambo ya makolo. Pano aliyense otukwana ndi kunyoza aMalawi akupatsidwa mpando kuphatikizapo mafumu. Koma zachisoni dzanja lalemba. Ngati munthuyu Mulungu akumusunga ndi moyo akufuna azaone kugwa kwake, koma akanakhala kuti anakawina ihhgg atamwalira kale. Bingu passed own coz kunakabwera zisankho akanawinanso.

Malemba Folo
Malemba Folo
6 years ago

Likhora you really have an ugly heart and you sound savagery. Mpasu was a president of his own party and belonged to opposition because that’s what he chose. Chakwera represents opposition in and outside parliament and therefore fit to speak on this particular function. What was government doing at the funeral of an opposition figure. Stupid minds and myopic people like you should use brains to think not your sick urine cool

Mtumbukash
6 years ago

Kikikiki chakwera wagwa nayo! Utuwa uwona sunati mfana. Maso khethekhethe ndiye umati ulankhule zako zamkutu zija? Hahaha dzipatse ulemu nyau iwe!

Zobanduka
6 years ago
Reply to  Mtumbukash

Wanyauyo anakubandulani 6-0 bwanji inu a DPP after wasting Govt resources kuti mwina kapena nkupezako olo mpando umodzi? Watch your mouth guys and tikumana mu 2019 momwemu umu pa ground lomwe mwagwa nalo lija mukhaula…… Kkkkkkk

Che Duli
Che Duli
6 years ago

Cha Chakwera ndi achipeta anzawo anyao kulilila kuti alalate pa maliro a eni ake….kkkkkkk

Zwellithin Sibanda
Zwellithin Sibanda
6 years ago

Speaker of national assembly was enough because the funeral was under government and precisely for Parliament.

Likhora
Likhora
6 years ago

This is the reason why mcp will never rule malawi again ,always crying for sympathy vote ,mumafuna kuti muyankhule ngati Mpaso anali wa Mcp? kapena mukufuna mavoti a ku Ntheu ,if that is the case go and hold a rally mukawawuze anthu nkhawa zanu ,ngati akakumvereni .

mlomwe was Ku MJ
6 years ago
Reply to  Likhora

Sizikugwirizana . Kungoti DPP is a primitive. This can only be done by poor country like Malawi. This was not a political party function. Umbuli ndiye umenewu.

Fortunately, u are giving Chakwera popularity.

An Eagle does not fight an ordinary bird….Chakwera is like an eagle.

Zobanduka
6 years ago
Reply to  Likhora

6-0 ija siinakukwanireni a DPP????? Watch your mouth you DPP idiots who always thinks backwards…..

Bandulo
6 years ago

That was great. Remember it’s Mcp that put him in jail without trial. He suffered in Jail .His death was contributed by the crocodile party. Who is Chakwera after all. Suti yogula pakaunjika
To hello Chakwera

Joji Wina
Joji Wina
6 years ago

useless article. Why always kupopa finye?.Chakwera ndiye ndani? Seeking sympathy basi kkkkk

Read previous post:
Malawi Police rescues Karonga eldery people suspected to be witches

Irate members of the community in the area of group village headman Mwangolera, Traditional Authority Kyungu in Karonga the northern...

Close