Email a copy of 'Chakwera ‘not bothered’ with Mutharika’s snub, cheer up Gwanda ' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

89 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Adzafunika
9 years ago

Amalawi timkanena kuti mtundu uwu ayi sianthu awa koma amalawi kumsamva komanso kupusa ndiye muone m’mene forex,mafuta,zisowere tsopano.Izi ndi zofuna dala amalawi musiyeni chakwera president wathu.

willywill831
willywill831
9 years ago

our people talk of education salvages, but ours is a proffesor salvage no wonder akupatsidwa mayina ndi ana.

Arthur G.M. Mtambo
9 years ago

MWINA DPP IKUCHITA MANYAZI NDIPONSO CHIFUNDO CHILI MU MITIMA MWAO NDI MAVUTO A CHISANKHO AJA, CHAKWERA CARRY ON AND GOD BE WITH YOU MAN OF GOD, PLEASE PRAY FOR MALAWI TO BE A LAND OF PEACE AND CALM + WEALTH—— KUCHOSA UPHAWI, NO CASHGATE AND CORRUPTION.

stephen
stephen
9 years ago

that’s my president. realy dont be bothered with such things. and im happy for u cheering mbuya, khazikitsani ubale wa ndii down there, zizatichitira ubwino 2019. plesdent okongola ndi mtima omwe.

stephen
stephen
9 years ago

that’s my president. realy dont be bothered with such things. and im happy for u cheering mbuya, khazikitsani ubale wa ndii down there, zizatichitira ubwino 2019

Zidura Ntengo Undigwere
Zidura Ntengo Undigwere
9 years ago

MCP supporters are obsessed with Chakwera, rather than the future of their party! Incredible. The cadres should be urging their leader to explore for future votes in the South; it’s not too early to start working to win the 2019 elections.
MCP have a lot of work cut out for them, to be sure. People still remember the noxious behavior of that party, the “nyakula” party, when it ruled in that proto-dictatorship of HKB!
Even at bao games in the villages these days, the mantra is: “never again, MCP” – a political statement one espouses after winning a game!

kamphulusa
kamphulusa
9 years ago

People like you are responsible for the ills this country is going through. You support people blindly. Umbuli a Malawi kumezera malobvu nyama yodya anthu ena. Tsopano mukuvutika chifukwa chakuba kwa anthu ena amene mukuwaombela m’manja. Muziona anzanu a ku Bukina Faso. Anthu adzuka ochenjela ogwirizana osati osankhana mitundu koma onse olira

Mwanamulanje walankhula.

If you Chakwera do not bother, then who does? You can’t do anything. Ask Tembo. Kuchita kuthawa ndale wosaununkha upuresidenti. History repeats itself. Its your turn for you Chakwera to dance political tunes and then finally quit presidentlessly. Usovenge.

Ronald Nkhoma
Ronald Nkhoma
9 years ago

ukamafa mumayamba ndimakutu kugontha

Kingpin
Kingpin
9 years ago

Why is APM bitter?? Ofcourse he knows tht Lazarus Chakwera is way better than him. We’ve seen ppo arguing on a daily basis in political circles bt it doesn’t get personal to this extent.He is being so very childish & this is NOT the type of leader we r looking for. We don’t have time for this. Serve wth the interest of the nation @ heart Mr President. Leave your hurtful emotions & misplaced egos to yourself!!!!!!

Vikhumbo
Vikhumbo
9 years ago

Inu Vomelezani,ku Opposition kulibe ulemu,mubamva kuwawa kumeneko ndi Chakwara wanuyo.angasiye ntchito yolumbira kufuna kutsogolela congress.tsoka ali nalo,zomwe anachita munthu ameneyu mukuti Chakwerayu zilingati munthu amene anakwatira mkazi wabwino ukwati woyera pamaso pamulungu kenako kuthesa banja kukakwatira Hule.Banja labwino ndi assembless,m’busa kuzozedwa thiii,mkuthawa kukakumana ndi hule opha anthu-congress,ife kwathu mau oti congress eeeeeee ndi mbola imeneyo,ndi uchite kuona tambala woti biiiiii umangodziwa mdza satana,inu chibweleleni tambala ameneyu nthawi yang’ona mpaka pano sanayerebe,zabwino palibe apa.munalamulira zaka 31 mwamavuvu,kuopposition zaka 21 mavuvu,musaiwale kumuwuza chakwerayo za 10 yrs yasalayo alimbe ntima,paja inu mumadalira ma 31.jst take not okufa sadziwika.

Read previous post:
Malawi netball giants Tigresses, Diamonds draw in OG Issa league

An end-to-end match between Complex Tigress and Diamonds produced some exciting netball as two teams settled for a draw  in...

Close