Email a copy of 'Chakwera is political lightweight, not a threat to DPP – Wa Jeffrey' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chakwera is political lightweight, not a threat to DPP – Wa Jeffrey' to a friend
Chitipa United’s below-average performance in the elite TNM Super League has attracted sympathy from Moyale Football Club Assistant Coach who...
MUNTHU ZOONA UNGASIYE UBUSA NDIKUKAYAMBA NDALE. ,.PENAPAKE KUMAGANIZA ABALE.
WHO CHEATED CHAKWERA HUTI AKHOZA KULAMULIRA MALAWI.AZAKHALA WAOPPOSITION
MPAKA KUTOPA.CHIPANI CHIMENECHI CHOSAFUNIKANSO KOLOWA M/ BOMA. TISAZAPEREKE DZIKO MMANJA MWA DEVIL GUYS.ZIANTHU ZONZUZA NGATI ZIMENEZI.
Kikkkkk mkwiyotu mudzimanaga nao, Man utsogoleri umafunika anthu oopa Mulungu mwanva? anthu amene ali ndi nzimu osati wofana ndi wanuwutu ayi!! kuteroko Satana aludziwa kuti dziko ili tsiku lina kaya mukufa ndi bp izo ndi zanu koma tsiku lina lidzakhala mmanja mwa olungama ndipo adzasangalala.
Pepanitu hahahahahaha!!
So why talk about him, if he is noone to fear. Why is she not talking of Chisi?
Stupid, idiots kukhala m’ma officemu kapena m’ma internet cafe mu kukhalira kuwerenga ndikumayankha Nyasatimes basi. Don’t you have anything to do apart from countering what is against you? Vindele nadi palijenso kujumpha apa yaye.
How can you win elections with votes from one region? Tapitani kumwera mukayese kukopa anthu kuti mwina mwake mungakokereko timavoti. Komatu mnzanuyu mukumuona akukulowerani kuchipinda chanucho ndiye inu nkumati akufuna adzabere mavoti koma nokha mukuona zochitika pa ground.
Signs of panic in DPP. This foul mouthed thieving woman, who is busy decampaining APM, a man whose image needs propping up, could do with Dental Formula Power
Alice Jeffrey mbava yothelatu…….munapanga history mayi
Just by mentioning him that is a surefire sign that Chakwera gives Dpp sleepless nights.If you were not bothered by Chakwera you wouldn’t be mentioning him. This Chakwera is really a threat to DPP.Muli madzi a DPP mu 2019.Kulibe Dausi kukaotcha ma box ama votes ndi winanso hacking phones to earn the votes for the failed Dpp.MCP moto!!!!!!!!!! Chakwera Woyeeee…..Wina alira. Jeff wa Jeffrey akumva kuwawa sanati….Mzake Kaliati ankafuna kugwa ndi BP analeka pano akungodya ma peyala ku constituency kwake ku Mulanje. Kodi ndale za pamalawi ndizamasewera?Osamazitengera pamgong’o.Bwinotu bwino..afunseni Atcheya akuwudzani.
Shameless sex worker talking.
Simple arithmetic!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Chakwera came number 2 with the votes mainly from the centre. Chakwera to win the elections he needs a good number of votes from south and north. Now, tell me where Chakwera will find the additional votes to win the presidency? Which district in the south is ready to vote Chakwera as their president? Which district in the north is showing readiness to vote for the party which started regionalism by sending all Tumbuka teachers to the north? Which constituency in the north will vote for a party which killed their beloved sons in the name of Dunduzu… Read more »
Holy Ghost Fire!!!!!!!
Signs of a failing government. Instead of letting the works of Peter speak themselves you are busy trying to cajole our minds into accepting that he is the best we have ever had. Unfortunately rationality is not good for politics.