Email a copy of 'Chanco MCP Wing to host a leadership seminar Saturday: Kunkuyu, Lunguzi to make presentations' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chanco MCP Wing to host a leadership seminar Saturday: Kunkuyu, Lunguzi to make presentations' to a friend
One of the country’s renowned gospel musicians has established an initiative called ‘Hold my hands; we educate girls’ with a...
Maunits you are indeed out of touch. Did multipartism reintroduced in Malawi in the 70s. Please be reminded in the 70s is when your Lion was made life president.
I stand by what I said kongilesi inazunza amalawi and this party must not be allowed to get anywhere near power.
Astikana mukafuna kupitiliza kuvala mabuluku musavotere MCP.
Up up The youth of Malawi. The youth unite to REMOVE MBAVA M’BOMA AND USHER IN SERVANT LEADERSHIP WITH A HUMANE HEART. THE FUTURE IS EVERYONE’S.
Nchani atsikana inu. Komadi Mwina mwabadwa nthawi ya matipate nkuona mukuombera mfiti mmanja. Lunguzi uyu bambo ake akangolowetsa ana ake ku secondary osasankhidwa. Amapanga school gate. Kupolisi ndiye Naja kugwiritsa ntchito lorry kunyamula zinthu zomangira mlangeni. Cashgate inaliko nthawi ya Kamuzu koma inalienable ya the untouchables ake Dedza. Wait and see.
kkkkkkkkk koma Hatton misala yeniyeni ndithu. Lero kuyerekeza ndi 1970 kkkk kagwere uko. Asiye anatchena awa sizija timaona zopenta zija ku dpp ichi ndiye chipani cheni cheni ichi
Azimai a kongilesi a Ku chanco mudzithokoza multipartism imene kongilesi siimaifuna. Nkutheka kuti ena inu munali musanabadwe, kongilesitu siimalora azimai kubvala mabuluku monga mwachitiramu. Ngati mufuna kuti kubvala mabuluku kupitilire, musadzavotere kongilesi.