Nyasa times please comment on the post from Mtolankhani, which story has the truth in it.
SUPER NATURAL MIRACLES
5 years ago
ANALI KU SCHOOL KAPENA KU
BANJA ??
Mtolakhani
5 years ago
A nyasa mumalemba khani musanafufuze bwanji? muzifufuza kae musanalembe, wakuuzani ndani kuti anafela mu room and it was blood pressure and mimba inali 7 months, Tadala wamwalilira ku chipatala ku General Hospital nthawi yochila and mwana anabadwa koma wakufa that time mkuti Tadala ali chikomokere mmene anatsitsimuka mkumva kuti mwana wake wamwalira z wen she wa shocked and passed away too
Sad
5 years ago
Very sad indeed, why was she not in the hospital after she was diagnosed with Preeclampsia??? That is an extremely serious condition in pregnancy
Kanyimbi265
5 years ago
Kodi iz zomati soul resting in peace munazitenga kuti???? I thought Bible limati wakufa saziwa kanthu biiiiiiiiiii? Passed on ndekuti chani? Kusawerenga mawu
Inetu I thought izizi ndizo chikristu chimaphunzitsa. Ife kwathuku akamwalira munthu timati, ‘kwa Allah ndko tinachokera ndipo kwa iye tonse tidzabwerera’. Mawu awa siodandaula koma ndi achikumbutso ndi chikhulupiliro
Justice
5 years ago
Sad development. What a loss at a tender age! May her precious soul rest in peace
It has to be “passed away” and not “passed on”. “When we say May his/her rest in peace” What do we mean? Other souls are not resting in peace?
Malaki 9:5-6 “Akufa sadziwa kanthu bi”…. Where was Jesus Christ during his 3 day death? He was somewhere? Where was Yona pamene anali m’mimba mwa chinsomba? Is the spirit immortal?
pass on. — phrasal verb with pass uk /pɑːs/ us /pæs/ verb. B2 polite expression for die verb : It’s important to remember friends and family who have passed on. Death and dying.
Nyasa times please comment on the post from Mtolankhani, which story has the truth in it.
ANALI KU SCHOOL KAPENA KU
BANJA ??
A nyasa mumalemba khani musanafufuze bwanji? muzifufuza kae musanalembe, wakuuzani ndani kuti anafela mu room and it was blood pressure and mimba inali 7 months, Tadala wamwalilira ku chipatala ku General Hospital nthawi yochila and mwana anabadwa koma wakufa that time mkuti Tadala ali chikomokere mmene anatsitsimuka mkumva kuti mwana wake wamwalira z wen she wa shocked and passed away too
Very sad indeed, why was she not in the hospital after she was diagnosed with Preeclampsia??? That is an extremely serious condition in pregnancy
Kodi iz zomati soul resting in peace munazitenga kuti???? I thought Bible limati wakufa saziwa kanthu biiiiiiiiiii? Passed on ndekuti chani? Kusawerenga mawu
I support you, nothing of such sort in the Bible.
Inetu I thought izizi ndizo chikristu chimaphunzitsa. Ife kwathuku akamwalira munthu timati, ‘kwa Allah ndko tinachokera ndipo kwa iye tonse tidzabwerera’. Mawu awa siodandaula koma ndi achikumbutso ndi chikhulupiliro
Sad development. What a loss at a tender age! May her precious soul rest in peace
It has to be “passed away” and not “passed on”. “When we say May his/her rest in peace” What do we mean? Other souls are not resting in peace?
Malaki 9:5-6 “Akufa sadziwa kanthu bi”…. Where was Jesus Christ during his 3 day death? He was somewhere? Where was Yona pamene anali m’mimba mwa chinsomba? Is the spirit immortal?
pass on. — phrasal verb with pass uk /pɑːs/ us /pæs/ verb. B2 polite expression for die verb : It’s important to remember friends and family who have passed on. Death and dying.
Mmmmm devil at work .May her soul rest in peace
Don’t blame the devil. Some how she was not careful herself.
A young woman getting pregnancy, dying with it, then we are blaming the devil. Really?
So sad… She seems to have been a strong woman.
Very Sad May Her Soul Rest in Peace
her souls rest in peace
Very sad. Was she not sharing her room with somebody else? It helps in emergency