Email a copy of 'Chande faces disciplinary action: Walks out after missing in starting line up' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

14 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MusandifunseZimemezo
MusandifunseZimemezo
7 years ago

When you feel you’re the best ndizenezi

Kalinchangu
Kalinchangu
7 years ago

Bullets yakulakwilani chani chande tinathana naye ndiwanu ameneyo izo waphunzira ndikuonera zomwe mumapanga inu kwanuko banja la bullets kulibe zimenezo mwakula mwatha muziona simunati

Hide
Hide
7 years ago

kkkkkk a Jaffalli chande kutelokutu carrier yanu ikutha pang,ono pang,ono koma sukumanya yayi kaya zako izo ife tikumango kumvera chisoni kutelo aakakuchotsa kumeneko ukupita ku mchengautuwa Fc kkkkkk

Good Samaritan
Good Samaritan
7 years ago

Osabweretsa khalidwe lachilendo laku Bullets kuno ai… Khalidwe lama Palestina kuno to-to! ! Kunotu ndiku chakwanu leka. Nomads players are well disciplined players and get instructions from the authority.

ndondwa
ndondwa
7 years ago

chande mumamufuna uja ndiameneyo ife tinkanena mwanayu ndiwamwano timangomusungira ulemu inu a nyerere mumvekere tapeza dolo tapeza dolo dolo lake lamwano wazaoneni ndiameneyo mumuziwa mwana wa sing’anga chande a ku Mitundu kkkkk

STEN
STEN
7 years ago

WWE DONT MISS HIM AT BULLETS

Tisachedwepo apa
Tisachedwepo apa
7 years ago

Penapake Chande mutu wake sumagwila bobo……handle him with care.

Trevor Chigwede
Trevor Chigwede
7 years ago

A Jafali Musayese ndinu akulu kuposa teamyo munachita bwino kuchoka ku Bullets

beje
beje
7 years ago

mwabwera ndi nkhalidwe loyipa ku noma munatengera Rasta George Nyirenda ? MWANO ASUTHANDIZA

Grant
Grant
7 years ago

zausilu bas chande usativute tikubweza upitaso ku BB

Read previous post:
Being bolder to do better on corruption in Malawi: British High Commissioner’s views

On May 12, the British Prime Minister David Cameron hosted the first ever anti-corruption summit. The summit recognised that corruption...

Close