Email a copy of 'Chande seeks court redress on Nyasa Bullets harassment' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
davie magaleta
davie magaleta
7 years ago

Chande musiyeni adzipita… koma ogamula nkhaniyi mukuchedwa kwambiri coz anthu ambiri tikudikira kuti timve kuti zathera apa. let the truth prevail kuti ena azachite manyazi

Chigwa
7 years ago

munsiye Chande

Chigwa Chimkhalo
Chigwa Chimkhalo
7 years ago

Musiyeni Chande musamuphere tsogolo inu a Sulom/ Fam mumachedwetsa chilungamo bwanji? Mukudikira Chani? Zaziii.

Peter Shidah
Peter Shidah
7 years ago

This Case Is Just Lack Off Good Approch

Athini
7 years ago

some are just commenting without understanding the whole saga is all about, these are the people who are misleading Chande, Chande be carefull your future is at stake here.

Ackim ckim kim
Ackim ckim kim
7 years ago

Achina Farao inu,muloleni munthu apite osati nkhazazo.Zimenezi mupangitsa kut musamasaine maplayer aluso bcoz azkhala ndi mantha kut ku BB kuli khomo lolowera lokha opanda lutulukila.

Macsedeck
Macsedeck
7 years ago

Koma Chitimu Ichi Cha Bibi Ndie Chipitedi Kuakwacha Ndithu Sory Zamanyazi

Andrew
Andrew
7 years ago

Sindinaone team,masapota komanso maofisho opusa ngati a Bullets padziko lapansi pano,simungatenge anthu achifwamba ndikuwayika mumpira,asasowetu mwanayu.

namalomba king
namalomba king
7 years ago

Tewesa kukamwa kumeneko…miti iyi ndiyoopsa m’bale wake ali ku 25 angosokoneza mpingo wa seveni,,,mfiti mapeto eishi….

big fish
big fish
7 years ago

Tewesa mwathawira kumpila mukufuna kuphanso anthu kumeneko. Mukuyesa nthawi ya UDF ino eti

Read previous post:
Kayerekela uranium tailing dams flooded: Water contamination fears high

The continuing heavy rains in Karonga have resulted in the flooding of Paladin’s Kayerekela Uranium Mine tailing dams, a development...

Close