Email a copy of 'Chaponda claims cash found stashed in suitcases belongs to DPP - Witness' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chaponda claims cash found stashed in suitcases belongs to DPP - Witness' to a friend
DR Congo’s AS Vita has launched mind games against Mighty Be Forward Wanderers ahead of thier first leg Confederation of African...
Woipa ngoipa basi olo mutamudzola zwitso!
Ma cadet olo mumuchemerera bwanji, Chaponda anaipa nkhope ndi khalidwe basi!
Who doesn’t lie in DPP?
Kodi achapondawa sachedwa kuyiwala akanama mabodza awowo. There was a time he said his source of foreign currency was because he had worked in various international organisations and also that he has children working abroad.
Ndiye mwadzidzi statement za gate collections from Blue night party zachokeranso kuti?
Ngwakuba Chaponda!
akulu awa alibe manyzi ndi bodza! DPP iribe bank account? why was the money in so many currencies? He is not only a thief but also aliar! these are the people who should not be anywhere near Government!!!
A mediocre BLUE party, patronised by the MULHAKHO BLUED testicled thieves, kusolora disgusting their BLUE midnight parties NO WONDER the country’s is in BLUES.
Ngati Hon. Dausi akufika potsutsana ndi mkuluyu, ndiye Chaponda nimunkhungu wakufipo.
Whoever thinks Chaponda will be arrested is wasting time.People hate him because he is super intelligent hence makin up stories against him. Graduate from Yale University. Si za makaladi apagalaja mu chikwawamu akufuna u veep ku MCP wa.
@ CALISTA CHINGOLA
KOMATU MAKALADI MUKWANENAWO ATA KUKUDYETSANI BWINO KUPOSA BAMBO AKO AMENE ALIBE NCHITO YABWINO KOMA KUMANGODALIRA MAGANYU M’MAKWALALAMU.
OLIVER IWEYO , WHAT PAPERS ( CERTIFICATES) ARE YOU HOLDING APART FROM BIRTH CERTIFICATE ? DOUBT NGATI ULI NDI BIRTH CERTIFICATE, SIZOMWEZI ZOTI UNANGOBADWILA M’ CHIMBUDZI.
KOMA IWE !!! BWINOTU BWINO…
Are u serious do u know how much it pains to be paying tax on the other end while you know that the monies will end into someone’s pocket why is it that we just support everything people Are dying in hospitals lacking medicine just because few greedy people like him had the audacity to still our sweat
Chaponda never graduated from Yale mu lomwe iwe, he is a graduate wa pa Zambia pompa apa!
Which sort of intelligence are you talking about? Of siphoning govt coffers? I don’t respect educated savages who lack integrity and a humane spirit. Another one is this dull Yale professor failing to steer the country forward.
Komanso kuAmerica uku ma Doctorate amakhala Ngati apa silver platter in some universities. Mwalamwala uli ku Britain. Obwera ku Oxford ndi ku Cambridge ndi azinzawo a mauniversity timapereka ulemu. Osati zinazi za ma Illuminati a skull and bones order (Yale), komwe kwachokera a George Bush ndi a John Kerry: anthu oipa kwabasi Ngati a Chaponda Chimanga ndi A Peter Mathanyula.
He is already arrested he is on bail
Anyapapi omapeka nkhani muyaluka! Chaponda ndi Boma ndi khethekhethe! DPP woye! Tikumvana zimenezo?
I see the cases against Chaponda going nowhere.The man is smart and innocent.
What makes him smart and innocent?
Cheap propaganda by the failing MCP which uses NyasaTimes And Times Group. Chaponda is winning the case and DPP is winning the elections next year.
Kodi mmayesa kale munkachita blame anthu akumpoto kuti ndi amene akudana naye chabe Chaponda. Lero nanga MCP through times and nyasa yaloweranso pati?
You see woipa ngoipa basi olo mutamuchita decorate bwanji sangakhalenso wabwino.