Email a copy of 'Chaponda collapses at DPP meeting ahead of convention: Malawi ruling party set for indaba' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chaponda collapses at DPP meeting ahead of convention: Malawi ruling party set for indaba' to a friend
Main opposition, the Malawi Congress Party (MCP) has bid farewell to its former vice president Richard Msowoya, saying the Speaker...
Kkkkkkkkkkkkkkkk I can’t stop laughing
Hahahahahaha, akanala wina adakhala chete kalekale. Pambiri yomwe ali nayo ya chimanga ija
You can’t still all that money and God remain silent it’s impossible you need to know what you have done to Malawians is painful
Haha yagwa atayifaka doom nsikidzi!
Mukanangomufinya pakhosi ali chikomokere apitilire kumanda. Anthu ambiri akufa chifukwa chambuzi imeneyi.
Abale Ku DPP kulidi democracy. Ku kongilesi amaitanizana pa whatsapp ati kuopa injakishoni. Abale demokalase yophunzirayiii!!!!. Pitani a kongilesi Ku konveshioni ya DPP mukaphunzire demokalase.
Your Undemocratic DPP is the one that sponsored the Kaliwo fool that threatened the MCP convention with an injection.
Umaidziwa democracy iwe? Bwanji mumachita mantha ndi Chilima ngatidi kuli democracy kuchipani chakocho iwe Mesimadzi?
mmmm za ziii a Mesimadzi ziti?
This is just the beginning. Mr Chaponda will collapse more and more til he’s no more. This is as a result of all the crying souls in Malawi that you have destroyed their destiny through your corrupt activities…stealing from poor Malawians and enriching yourself…REPENT REPENT REPENT
Kkkkkkkkk sanati iyayi tiye nazoni nkhalambazi one after another all they know is stealing. Ma BP ake amenewa nde mulimba ? Kulili a Minister of finance athu nde adzangofelatutu hahahahaha akakhala atsogoleli athu ndiye paja inawathyola kaye stroke!
You could have allowed the same to happen for the position of the president then you could have seen the true colours of DPP supporters. But you did not want Peter to be challenged.
Wakhuta chimanga chakuba ameneyo
Abale mpaka comokalization…. Thapatula zisiye izi utayisa moyo wako sure. Support ulibe iwe uzimva