Email a copy of 'Chaponda visits Malawi xenophobia victims in South Africa: ‘Skills for work courses for returnees'' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

42 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
godfrey
godfrey
8 years ago

Dziko lathu ndi losauka ntchito ikapezeka kulembana pa ubale

abdallah
8 years ago

Mutatimangila ma company zigawo zonse zikanankhalako bwino mwine mkunthawako mabvuto alikunowa. Lero lino tikubvutika kuno kamba kakusowa ntcito ku mudzi.

John myths
John myths
8 years ago

they are no south Africans in Malawi so do u know wht does tht mean?….It means .We are no living I poverty country

JONES KANYUNDO
JONES KANYUNDO
8 years ago

guys zibwerani zinthuzi akukolezera ndi Zuma tamva kale mau ake a pa 28-4-15 sakufuna wobwera kumeneko.

juma ngwira
juma ngwira
8 years ago

Koma ndizovesa chisoni,boma likufuna kusegula ma xool kamba ka xenophobia kale anali kuti kupanga zimenezo ayi basi tathokoza pitiliza. Maganizo ano abwinowo

Kenneth leonnard
Kenneth leonnard
8 years ago

I ever been in RSA and what happens now is like cheating each other

Naliyela
Naliyela
8 years ago

wamakani akhale ku South konko.kwanu nkwanu ,,,,kuzolowera ukapolo eti?a Malawi ambiri tinazolowera kuzunzidwa,,,kupilira zosayenera kupilira,,zibweraniko uko.tikumvatu zambiri kuti enanu mumagona malo omvetsa chisoni ngati pansi pa ma brigde.Ngati mukupanga ndalama zambiri bwanji osapeza nyumba.shupiti zibweraniko musanyozetse dziko.ma bus ndi amenewo aulere kwerani tikukudikirani kuno kumudzi.sakufunsaninso za passport.By the way kODI KU JOBERG MA BUS SAPITA/A

Oesley
8 years ago

Panopa Kuno Amene Tikusowa Ntchito Tilipo Ambili Komaso Maphuziro A Community College Akufuna Ndalama Kodi Ndalama Zoti Tilipilile Ma Kollege Tizitenga Kuti Tili Pa Ulova.

Tulo
Tulo
8 years ago

Chaponda does not know what he is talking about. There are no jobs in Malawi. In South Africa there is a job for everyone. Imagine munthu wosesa (gardner)kulandila R3000 (K120 000) pa mwezi. No wonder people flock there.

Malawians also create their won work by selling vegatables or fruits. They can make a much as R4500 per month.

Malindima
Malindima
8 years ago

He already said that chuma chiri mu nthaka! Many foreign markets want soya beans, chalimbana, uchi, nandolo, nyemba and many other crops.
You will learn the basics of farming at community colleges and each one of you will be given hoes,watercans, water pumps and you will be encouraged to grow commercial crops so that you can sell and make money!
So come back home; xenophobia will not cease. The owners in RSA are also jobless and thus why they will never stop killing us there.
Together we can build Malawi to become another Malaysia!

Read previous post:
CSOs welcome Malawi govt’s historic appearance at African Commission

Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) and Centre for Development of People (Cedep) have applauded Malawi government’s historical appearance...

Close