Email a copy of 'Chatinkha appears at govt function, says not yet joined DPP' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
JERE-MANDERING CHIDZANJA CHA DPP

Chidzanja chakuba ndrama za boma chikusoneza politics pa mudzi…kugula yanthu yonse kuti anene kuti …atenthani nsalu ya kamuzu.

Shithole Country
6 years ago

Who was Chatinkha in MCP? What impact has her departure made on MCP. Nothing and literally nothing. Is DPP really helping Malawians? Is what Goodall Gondwe did by trying to steal our taxes amounting to K4 billlion good? How many schools could that build in the North? The old man is becoming a children and licking the boots of Pitala.

Hatton
Hatton
6 years ago

Mdima umadana ndi kuwala. Mzosatheka kuti kuwala kukhale Ku MCP chifukwa MCP ndi chipani cha Mdima komanso chakupha. Onse odana ndi mdima ndi Omwe akuchokawa.
Anthu onse okonda mdima ndi kupha adakalibe mu MCP.
Ndikufunirani mafuno abwino nonse amene mwasiyana ndi mdima. Musaope chifukwa Mulungu, yemwe anthu ena anamuthawa ndi kukalowa mu mdima, akuyang’anirani.

Agenda Setting Theory
Agenda Setting Theory
6 years ago

Chatinkha Nkhoma. attending as a cotton farmer???? just tell the truth, you have joined DPP. it is sad that DPP can welcome a violent woman like you. What you did in burning MCP cloth was an act of violence. I don’t think anyone who has left a political part for another has done that. DPP should be worried to be associating itself with this women. She demonstrated o the whole nation what she is capable of doing when things don’t go her way. You give her a platform at your own peril.

Youna
Youna
6 years ago

Zilibwino atichoka. Akasokonezeno ku Blue camp.

koma kumeko
koma kumeko
6 years ago

They have accomplished their tasks, now its time to come to the open to show their true colours. Its time to sell themselves under Dpp. I hope they were already promised that they will stand for Dpp in 2019. That is why they were doing whatever they have been doing. Sizodabwisa… koma nkhanga zinaona kale.

Funga
Funga
6 years ago
Reply to  koma kumeko

Chatinkha is good riddance and her leaving was long overdue. Sitifuna zigawenga ife in our new MCP. Let her go and rot with DPP, harlot, jezebel

NGWENYA
NGWENYA
6 years ago

Nonseenu mukukangana apa inu siyanani. zikhwaya izi zonse zikulowa kwathu kuno musadandaule nazo zatha basi. chifukwa sitingalore kuzipatsa consitituency momaliza muno nthawi yonsesyi zakhala zikutinena. Mau ndiomwe ananena Nankhumwa uja anthuwa asatisokonezei!!!!!!!! tiwaika kaye akakhale branch governors kkkkk

Borne
Borne
6 years ago

Mkadzi wa DPP uyu very compatible with her lover. She’s have been a brand ambassador marketing propaganda for her lover on MBC.

Central
Central
6 years ago

Mimbulu yonse kuonekela poyera…………………………………………………….. mumati mutani! Nanga mumafuna mupusitse ndani! Apatu mwapusa nokha……..! Pano muti chiani tsopano, paja mumakana kuti ndinu a DPP koma kumanamizila kuti ndinu a MCP!! Ana a njoka inu, and you don’t have morals………………………………………. Mulowa zipani zingati? Why being pompous for nothing! Mpakana chipani ndi cha bambo anga!! Eeeeeeeeeeeeeeeeeeeee mwayesa munda…………….. wa kwanu! Chipani cha MCP ndichosiyana ndi DPP, UDF and PP. MCP ndi ya mamembala ake pamene zinazi eni ake ndi aku banja………………………….. basitu ndi chifukwa utsogoleri ndi nkhani ya ku magazi! Kuteroko a change golo awonanso zija zowalanda galimoto muja zidachitkira akupereka ma certificate… Read more »

kaka ni dada
kaka ni dada
6 years ago

Mbava zimadziwana kolowela

Pitala
Pitala
6 years ago
Reply to  kaka ni dada

Zoonadi mfiti zimadziwana next house koti zikatambire. Chatinkha was claiming kuti MCP nja bambo ake? Kkkkkkkkkkk adamuuza kuti Kamuzu adali ndi mwana ndani? So you wanted to be treated with kids gloves? Wkhaula hule wachabechabe ng’ooooooo!!!

Read previous post:
Jubilee University launched in Malawi: Determined to offer relevant programmes, transform citizens

Jubilee University—one of the latest private universities in the country that was unveiled by Vice President Saulos Chilima—says it feels...

Close