Email a copy of 'Chidzanja backs Chakwera-Mia pair in 2019, dismisses electoral alliance' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chidzanja backs Chakwera-Mia pair in 2019, dismisses electoral alliance' to a friend
The Women Lawyers Association of Malawi (WLA) are still putting pressure on President Peter Mutharika to rescind his appointment of ruling Democrtaic...
Was so amazing congregation with just a short notice….
A Auga Chidzanja mukukumbukila muli pa
Mitundu Secondary munkakapereka soap kwa a Khukhi kuti azikupatsani zakudya zambiri, what will stop you from corruption mukazalowa mboma?
MCP ikazalowanso m’boma , Kamuzu azadzuka kumanda.
..Lunguzi Should go as MP for dedza like Kabwira. the lakeside committee shouldn’t cheat mcp national executive
Chidzanja, like his distant cousin Chatinkha, is a confusionist
They sound very foreign?What about Peter?
I agree, Peter is no better. The only good communicator is Chilima.
Ukusiya ofunika translation uja. Amalakhula ngati mkanwamu muli dzila lamoto. Pena akamalakhula munthu umayesesa kuyang’ana mkamwa ngati mulinano. Gogo yafikakapo.
Chidzanja is a disgrace to MCP.
He is indeed a disgrace. He should stop harrasing Juliana and Jessie who are the strongest women in MCP and the whole parliament. We in Dedza east love Juliana. Chidzanja’s problem is that he has already eaten bribes from other people, please Chakwera and Mia remove this pest adzagwetsa boma lanu.
This pair sounds very foreign when you listen to them speak, may need translators.
Its purely understandable to hear those who stayed over 40 years in chicago, America when they fail to clearly understand some pure Malawian vernacular! Abale 40 years si panotu!! Musadandaule bigman mwina mudzayamba kuwamva bwinobwino anthuwa akalowa m’boma on 21 May 2019. Nanga si pa nthawiyo adzakhala akulankhula ku mtundu wa a Malawi frequently! Just be patient bigman……………………………..!
Bigman iwe sukudziwa kuti ena asankha kumachita zao kuthawa m’boma chifukwa akuthawa zomwezooooooooooooooo zosamamvetsetsanazo!! Ndinu alendo baba……………………………………………….. munazolowela zina mchifukwa mumalankhula ngati mwavumata “Hotdog”! kikikikiki Ifenso timavutika nanu kukumvani man……………..!
kodi mwati MCP idzalowa m’boma? kkkk.. Tidzakhala tikumva mbwelera za ‘atibera’ just after May 21. Palibe chomwe angaphule awa
U R A LIAR BOSS.
Kikikikikikiki
Vuto lako ndi School. U need to go back for kwacha classes