Email a copy of 'Chief Mwalweni of Rumphi campaigns for DPP in total defiance of electoral laws' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chief Mwalweni of Rumphi campaigns for DPP in total defiance of electoral laws' to a friend
Minister of Information and Communications Technology Henry Mussa has said government is pleased with head of the influential Roman Catholic...
Mfumu ya Chitumbuka. itavala duku ngati namfedwa. Eshhh kumpoto ziliko
DPP boma
Mafumu openya awa akudziwa zombie boma lawapangira, simungawatseke pakamwa ai. True has to be told. Mafumu amaona zombie zikuchitika, osati Isi mungotsusa koma simukuona ai. Keep up Senior Chief, afootokozereni anthu chilungamo, you sherperd them.
As expected, MEC will be clueless on how to handle this matter. Remember DPP has 5 Commissioners in MEC, they cannot bite the hand that feeds them . The commissioners will bury their ugly faces in the sand and pretend nothing happened.
What a shame!
These chiefs are intimidated by the government officials. They are forced to do things against their conscience. It’s all because of poverty. Poverty is the root of all the evil. Poverty drives people into criminal activities. Poverty drives women inti prostitution. Poverty breaks marriages. Poverty takes Uladi Mussa to different parties. Poverty is keeping Ntaba in dpp. Poverty is evil.
Nanunso chilichonse intimidation by government. Munthu asanene za kukhosi, asanene chilungamo waopysedwa ndi boma. Inu akukuopyesani osutsa boma. Let the chief help his people to do right thing, osati chifukwa inu milk ndi kanduka ndiye munyoze a mafumu.
Nothing will happen to this defiant traditional leader. Koma akanapanga endorse an opposition figure eg Dr Laz Chakwera, Saulosi Claus Chilima, pompo-pompo akanagwidwa ndipo tonse tikanati MEC inachenjeza za izi. MEC will be toothless on those glorifying the ruling elite. Search me
A Wilson, tamangodyani basi inu muzawatani mafumu world, ndiye kuopsezako kumeneko. Inu mukawakhazike pansi a mfumu, mwakulira kuti inu.
Malawi Electoral Commission ili pheeeee! Anayamba ndi uyu wa ku Chikwawa Lundu, pano ndi uyu Mwalweni! Demeti
Tsono MEC itani ndi a galatiya opusa ndi aneneri onyenga amati mvotereni lazaro aja?
Kkkkkkkkkkkkkk kuwaona a Mwalweni wo iiiiii atichimwitsapo iyaaaaa……………….
KAPILIKONI mwenecho, utijiwonere wekha pala dazi lafika, 21/5. Lyaninge vyanthontho, ulunji wasuzga.
He is a stupid chief.
He can not be stupid because he has mind his views known. This is democracy, we differ, but that does not make you stupid, mukuyenera kulandira mwambo a vinjenje, manga mwa dzina Kanu. Mukufunika mupite kudambwe, kapena kuti ba, kundagala mukaphunzire chikhalidwe. Sititukwana mafumu chifukwa tasiyana Nasongole maganizo.
Afumuwo ndambwiyako?? M’mene atukwanila Lundu pamsokhano iwe ukuyembekeza kuti anthu asamuyakhe?? Ndindani iye simunthu?? Ayakhidwa basi kaya ndi azigogo ako izo ndizako