Email a copy of 'Chief Ngolongoliwa says Kaliati accuses Mulli of dating her daughter' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

25 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
wapachala ngwaphepo
5 years ago

A UTM nzanuyo olo mukulimbana naye koma ndi katakwe, jealous down, jekete sapisira khwani saotchera. Zoti azungu anatinyanyala palibe chomwe chinaoneka, miseu, state of art buildings izo!….zoti kunali chin’gamba chotsatidzana ñdi mvula yoononga, ayi ndithu, chimanga chili bwee, low malnutrition levels in the NRU, low malaria cases, uku azungu akankumavula zipewa nkumamtaila kamtengo APM. Nsanje, bodza ndi dyera sizitithandidza a malawi. Zoti ma civil servants aman’gamba calender zinanka ndi miss cashgate komatu zonsezo muzero aid. Kuonjezera ma salary mmy July, Julyyemweyo maincreament anthu kulandira osati zamaarrears. Okoma aatani onga fungwe.

inspector wa UTM
5 years ago

Akaliati apa zikuoneka ngati mukulira Mulli ndi paramount Ngolongoliwa atakusasani pabodza lomwe munawaneneza ku UTM kuja. Ndiye munadzazidwa ndi mkwiyo. Inu a UTM musamaphatize za mlakho ndi ndale. Nthawi ya amayi alomwe anavutika koopsa pazifukwa zopanda mitu ngati izi. Inu mukutiuza kuti pa ana 100 aliwonse 95 amzeru amachokera kujaku? Quota system ndi dhiru chifukwa enawo amangokonderana. Komanso mutisiye osaukafe tisakhale nyambo yanu yopezera mavoti kuti inu ndimawanja anu mudziufira. Ndiliti munayamba kutokota za osauka? Nanga bwanji mwatha zaka migolo migolo kuparliament koma olo nditsiku limodzi lomwe osatikhazikitsira mfundo zotithandiza, ena ndiye mpaka u first lady koma njeee palibe chomwe… Read more »

NERAIN
NERAIN
5 years ago

Politics without direction are the source of uncivilization. There is no respect from the mouth of ignorant politicians. UTM stop mixing politics with family affairs because Malawians only recognise you as leaders. How will you lead the people if you lack respect for the elders? Chiefs sit down with children to give them good counsel and direction so that they may be good leaders of tomorrow; don’t argue with children because you will be put to shame as a Chief.

The Patriot
The Patriot
5 years ago

One day a non Lhomwe will rule this country and verily, verily I say unto all Malawians that at that point in time the Lhomwe belt will understand what nepotism can do! Ngongoliwa will no longer hold the priveledged position that he is holding now. Mulhako has involved itself in politics too much that if DPP will lose in elections next year the whole tribe will weep and wail. It has reached a point where the tribes most celebrated achievement in life is producing rulers!! Guys be serious, get a life . There is life outside government dont behave as… Read more »

#DzukaniAmalawi
#DzukaniAmalawi
5 years ago

Chief Ngolongoliwa, is this something you’d want to disclose the public and lay bare your subjects confidential matters. Malawians are hungry, poor and living in grass houses and all you can voice to the public is some confidential discussions with Kaliati. A good chief isn’t supposed to be a gossiper but someone who can trusted to a confidant. Why would you sell your soul and integrity for a few Kwachas. Please introspect critically and change your ways and become the chief that your subjects expect.

Chisyano
Chisyano
5 years ago

Mulli is a married man. He is married to Malawian woman and he also has a Chinese wife. Any mother, in P. Kaliati’s position would not want her daughter to be seduced, duped and used as a sexual object by a useless womanizer and fornicator.

Central
Central
5 years ago

So the CEO wants a vigil for the blockade Kaliati is building against his chair’s thimbwizaaaaaaaaaaa kikikikikikikikikikikikikikiki, umveeeeeeeeeee heavyyyyyyyyyy ku mulhakhooooooooooooooooo

Mesimadzi
Mesimadzi
5 years ago

Mai Kaliati anayenera kudziwa kuti Ali ndi mphamvu komanso ulamuliro pa mwana waoyo osati pa Mulli ai. Maiwo amuuze mwana waoyo kuti asiye kuyenda ndi Mulli osati zimene akuchita zolubwalubwa poimbila anthu ena mafoni. Komanso maiwa akanatha kuchita ndi Mulli zija anachita ndi mzimayi yemwe amamuganizira kuti akuyenda ndi amunawo. Mai Kaliati anamuvula mzimayi nzaoyo ndi kumakalibusa amuna ofuna mzimayi. Nkhaniyi imafanana ndi zomwe anachita azimai ena Ku Lilongwe. Chodabwitsa ndi choti mabungwe onse omenyera ufulu wa amai sanachitepo kanthu. Timufunafuna mzimayi amene uja ndi cholinga choti Chilungamo chioneke; nkhani siyiola. Mai Kaliati muvuleni Mulliyo ndipo muzikalibusa amai ofuna amuna… Read more »

icho
icho
5 years ago

I think Ngolongoliwa knows more and the sincerity of Kaliati’s outbursts. According to how he has responded am sure him and mulli once told kaliati to rally behind chilima because the way I know ngolongoliwa , he would have been very vocal on this issue than the he has done considering his loyalty to peter mutharika but he knows that saying too much on this issue will make kaliati reveal more on the issue since he know very well that kaliati alibe chibwana or mantha. Anyway za alomwe is chipasupasu while eating kalongonda okhaokha.

Mwananyanian
Mwananyanian
5 years ago

Here is the most pertinent question: Is Akweni Kaliati’s daughter of age of consent? If so, why does the mom feel obligated to stop the “friendship”? Unless she can prove some nefarious motives.
Is this one reason Akweni has soured on DPP, the Party that made her who she is as a politician?

Read previous post:
FND calls for Speaker Msowoya to resign  over Section 65

Forum for National Development (FND) which is reportedly being bankrolled by the State machinery, has asked Speaker of Malawi's National...

Close