Email a copy of 'Chilima rescue patients awaiting brain scans at Queen's Hospital, donates K1 million' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

43 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Thyolo Thava boy
5 years ago

God bless you Dr Chilima, you didn`t blow the trumpet for this assistant. The public hospital seems to lack the line minister because when the hospital authorities complain to the Ministry of Health they are referred to the councils, kodi ndalama zama phasi mungayendetsere chipatala??? Boma latayilira ili iiiii. 2019 amalawi tiwereza sitingalole kuti tipitilize kukhala chonchi

Cole
Cole
5 years ago

I am more impressive with what the Vice President has done. Indeed a leader must always be touched with people’s lives. I have an experience with Dr. Kamalos’ dept. It’s quite a very sensitive dept for people’s lives. Well done Chilima

Nani
Nani
5 years ago

All these are campaign gimmicks. Chilima has said he is part of government, so what is his government doing?

Austin
5 years ago
Reply to  Nani

Work up stop! talking Nonsense this is really a merciful job???????

Zameer wa MuthariKarim
Zameer wa MuthariKarim
5 years ago

Free advice to APM, Nankhumwa & Company: Athandizeni anthu pamene akudwala osadikira akafa kuti mukaSHAYINE pa maliro awo. May the Good Lord bless you SKC.

Godfrey w. Nantali
5 years ago

Enanu ntchito kulimbirana munthu wakufa kale , kodi wamoyo ndi wakufa wofunika chithandizo ndiye uti ? Anthu A DPP mitu yanu nonse yosagwira . Kampeni pamaliro , aaaaa pepani kwambiri . Nanunso a ACB mukufunamutiuze chani , munayamba mwamanga anthu, zachamba basi. Pamaene mwaona kuti zisankho zayandikira mwayamba kutinunkhisa nkamwa , munamanga ndani pa Malawi pano ? Osangokhala chete bwanji ? Nanga amane anaba chimanga uja mwamusiiranji ? Nanaga uja waba K145, 000, 000.00 mwamusiiranji ? Mukuyesa a Malawi sakuwona eti , muzaziona , mupemphere zolimba kuti mbuyanuyo asaluze , koma akangoluza inunso kumeneko muzatiimva, ndipo muzidyeratu panopa , tizakumana… Read more »

Godfrey w. Nantali
5 years ago

Mr Chilima , our 2019 Prezident , mumatiimirira, mwapulumusa dziko osati munthu mmodzi ayi. Mulungu akusungeni mpaka May 2019 , voti yanga ndakupasani kale musadandaule ayi .

Omega
Omega
5 years ago

Patapezeka anthu oterewa okwana 145, tingapeze K145,000,000.00 yothandizila zipatala zingapo.

nambewe
nambewe
5 years ago

Awa nde a president amene ndimawadziwa ine UTM 2019 fireeeeeeeeee!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Chriss
Chriss
5 years ago

Timva ma transfer ndithu pamenepa, zaziiiii

jossee
jossee
5 years ago
Reply to  Chriss

Sukunama ase ,timvadi

Word of Advise
Word of Advise
5 years ago

Lets do cloud Funding. Amalawi titagwilizana we can even buy a machine for thevgovt hospital.

Fundraising activities
Whatever brings money.. With Good planning and Unity we can raise money to buy machines.

The problem is TRUST.

Damalara
Damalara
5 years ago
Reply to  Word of Advise

Sure uko ndiye kukhala bwana Chilima Vote yanu ndinabwera kale kudzadula ndili nayo ku capetown. Akakwana masiku ndidzabwera nayo.

Read previous post:
Chaotic traffic jam in Blantyre : Makata Road closed

Blantyre streets caught in worst traffic jam crisis because of closure of one main link road; Roads Authority assures of...

Close