Email a copy of 'Chilima to grace ‘Kuwala Night’: To hold UTM rally in Nkhotakota' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chilima to grace ‘Kuwala Night’: To hold UTM rally in Nkhotakota' to a friend
Political nomad Salim Bagus has quit main opposition, Malawi Congress Party (MCP) as second deputy secretay general and withdrew his...
Look at that logo, it is saying united transformation movement, koma pa nkhani yakukoti akuti UTM siikutanthauza chomwecho. Crook number one, Please bring that evidence to court.
MOTO WAMAPESIIII!
ukuphani sure.
UTM ndi dhuuu
These are the things that are promoting corruption. Most of the money will be coming from corruption sources.
Corrupt minds will always thing negative. Koma aziti blue night where people and organisations are forced to contribute money. AMalawi tizayamika liti zabwino. Anzanu akupitiza kulemela ndi ndalama akukuberanizi inu mapazi ali mbu
oMachemba will be in the company of others in KK, to observe and report the size of the audience, enthusiasm and will ask many who have registered and actually intend to vote UTM (degree of commitment).
Fair enough?
MUMATI CHANI APHUMBWA INU MUZIWASO NDE BY FRIDAY JUDGE AKUGAMULASO KUTI UTM NOW IS REGISTERED AS PATY
kkkkkkkk trip ya ku Nigeria yapindula, misonkhano ipitilire tsopano timve mabodza
Cadet iwe uli ndi pension ndithu, ayayayaya
kkkkkkk iwe umati bwa? Zocheza izi ada, kungotayitsapo nthawi
Cadet iwe uli ndi pension ndithu ayayaya
You are saying the dinner dance will take place in Blantyre, but you don’t specify the place, Something is fishy with these drunkards.
cholinga mukaziwako mukasokoneze issa ! eniakefe tikuyiziwa venue
Kutereku mukufuna mukabisalire ndizikwanjekapena mukawamenye eniake a malowo.
mukufuna mukawakhape ndi a pwitika anu ajaaa, eni ake tikudziwako. We surely dont need single cadet there.
The people who matter and need to know already do so,
we wish you all the best the vice president , and we are behind you papa
NANGA ZA MACHINE OSOWA OPEZEKAWA ZIKUTI BWANJI ??