Email a copy of 'Chilima warns MRA, Macra bosses on funding DPP campaign: Abuse of public resources' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chilima warns MRA, Macra bosses on funding DPP campaign: Abuse of public resources' to a friend
As a way of controlling the gaffes at the governing Democratic Progressive Party (DPP) the party ruffians on Sunday started confisticating...
Mbambande chilima
AChilima mukuona chitsotso mdiso la anzanu pamene mdiso mwanu muli chimtengo. Inu abwana si amene mukulandira salary yaulere, nyumba yaulere, security yaulere pa misonkho ya a Malawi? When did you last perform government duties and yet still on government payroll and calling yourself VP? Uyambe ndiwe kubweza ndalama za misonkho yathu!!!
Sukudzuwa chomwe ukunena iwe
Ankolo ndekuti mukuvomeleza kuti diso ilolo muli ZITSOTSO? hahaha
Chitsiru cha munthu ichi chakuba misonkho ya A Malawi. Tuluka nyumba ya boma if people are to trust you. You failed to campaign for a bi election in mchinji when you were Vice President now you think you can campaign for a party in the entire country and win an election ??? never. Mary mkazi wako waiona game patali wasiya Kuyenda nawe. All your people are failing to campaign on their own no funds . Look st your friends In Dpp they are everywhere akazawina muzizati abera. Mu lira simunati
umbuli wanu bwana osamaulengeza choncho
Mr vice president you set a wrong button. You also draw salary and allowance for no apparent reason. Chabwino if you are serous report to ACB for action
APM and Chilima you are crooks. So you agreed to separate aliyense azipanga payekha to confuse us as you are two parties but funded from same pocket through government departments and ministers.
Mupusitsa anzanu omwe adali a DPP.
The same Vice President is using Taxpayers monies. Double standards… come on honorable your motorcade, salary, allowance, security personnel etc You were elected in DPP & sharing convenience at the expense of suffering the Malawians.
AKAMAKUDZUNGUZANI A DPP NDIAMANTHA MUZINGOTI DIPETI !!!OSE MUONA ANTHAWA NDIAMATHA INE NDIMANGOKUWA DIPETI !!!!! NDIKAMADZUKA NDIMAPEZA ANTHAWA NDIZISILUTU TIAFINYA PA21 POTI AMAKOMAKO PAFUPIPAFUPI INU MUKUZIWAKALE NDIKAFANDALA SIPATA WIKI
bwana chilima inu phe akanganyawa achuluka mbomamu tisileni ine tikuziwa pongwela oloko mutao phyetsa kuti dipeti anthawa koma ena abwelela ndizosava zilombozi takozekela pa21 pano pamene aziwe kuti ifeso aboma tinatopanazo inuphee
Iwenso ukulandira salary ya ulere osagwira ntchito ya boma. You are campaigning daily for your party but getting paid by tax payer money, free housing and free security. You have no moral ground to question anyone on Gov resources
Inu boma linasiya kumulipira kalekale Chilima check with the Capital Hill records. Mumangonena zinthu osadzidziwa,
George, Chilima went to court arguing that government could not take away his entitlement. He is getting free salary without working, security detail, allowances, transport etc. Chilima is simply a thief
Musayambe ma lemu excuses pamene mwawona kuti ground sili bwino.Mumayesa zopweka tiye nazo