Email a copy of 'Chimango Kayira hints at Nyasa Bullets return' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chimango Kayira hints at Nyasa Bullets return' to a friend
Malawi champions Nyasa Big Bullets FC have navigated through their current crisis by accepting all conditions their sponsor Nyasa Manufacturing...
Tikulandilani a Chimango ,Bullets ndikholo lako palibenso kwina komwe ungapite.Nowadays Bullets is the best.
Welcome back Blackberry nthawiyo ikakwana. Enawo akuopa that’s why they can comment negatively.
Waona kuti Alfonso Djakama ndi abale ache akufuna kuthira onga kumeneko nde wati eee! Phazi thandize! Ku bullets anthu akusaukabetu, mukapirira?
Welcome back but musadzachitenso chipongwe pochoka. Pamsasa saipitsa achimwene.
Kodi black berry akuthawa renamo kapena wamva kuti kwabwera nsuzi ku bb.bweranikoni kumpanyirako akuphani a renamo
welcome back BlackBerry takulandira
Meticashi yayamba kunukha mfuti…kkkkkkk!!Bwelaniko basi mudzidzamenya waphuphuphu womwewu..munatha kale mpira munkamenya ku secondary!
ZITSIRU INU MUKUNYOZA ANTHU ABWINO CHIFUKWA CHA DICTATOR SAM. MA PLAYER A BB NDINU MBULI NONSE .
MUKUFUNA KUTI TEAM AZIYENDESA MUNTHU MMODZI ,DIKIRANI MUZIONA.
MUZAWAFUNA ANTHU MUKUWANYOZA LEROWA ZITAKUGWIRANI PAKHOSI.
Siuja amati BB imusaukitsa uja uyu, lero zatani?
welcome aboard our terrific midman