Email a copy of 'Chinsinga receives death threats for being critical to Mutharika govt: Malawi political analyst' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Chinsinga receives death threats for being critical to Mutharika govt: Malawi political analyst' to a friend
Malawi Police have arrested four people in connection to the violence that erupted on Sunday at a solidarity rally Malawi...
Mr Chinsinga’s comments are completely true and so help him God..since 1994 mpaka pano dziko lathu la Malawi mapulezident wonsewa mbola zokhazokha zikanakhala mbewu tikadati mbewu za research..Onsewa akulowa m,boma popanda vision kuti azapanga chani.Chinsinga wanena kuti mapulezidenti onsewa ndi ma try and error kodi akunama? Uyu alipoyu wawonjeza kaya….
I dont agree with the way the DPP is running government buy I think kunyoza kwinaku ndikoyenjeza based on personal hatred!
We have had only one accidental president in Nyasaland by the name of Joyce Banda! The rest campaigned and were voted into office so osamangoti fwiko fwiko apa!
pipo what r u complaining about?? Mukufuna azichita kukudyetsan mmakomo mwanu Peter yo!!!!Amene ulamuliro wake ukumunyasa ayimitse chala chakuphazi mmwamba.
Kkkkkkkk This fool Chinsinga is afraid of his own shadow.
Zophana sibwino. Ine sindimasapoter chipani chilichonse koma a dpp musamasowese anthu mutendere. Mukazachoka anzanu azapange chonchi mzasangalala? Kwacha yatha mphamvu . Anthu akamati muchoke amafuna kuti mwina mungasinthe zinthu koma inu muli busy kumawopyeza anthu. Apm simulungu azachoka anthu akazafuna
What good has ever come from DPP? APM and his entourage are a typical of a clueless bunch of opportunists hand-picked by corrupt failed lawyers into govt. They think they’re in heaven but living in hell. Only time will tell.
apm is great!chinsinga should take functional approach other than confusionism approach.he is full of theories.
ACHISINGA INU OSANGOYAMBITSA CHIPANI CHANU MWINA MUKADZAWINA MUTSOGOLERERE DZIKO LA MALAWI MPAKA KULEMERA BWNJI
A Bwana President,afune Asafune,u Are And Will Be Our President Up To 2O24.Beliv Me.U Cant Be 100%&none Is In Life.Just Be FreeLet Them Talk,70% Of Malawians Are Behind U.Mzakwacha Nixon->+27731440799,306 Retif Strt Pretoria.
Leave APM&DPP Self.If U Want,campagin And Dislodge In Through Vote In 2O19.Malawi Must Be Ruled By Peter Up To 2O24.Mzakwacha Nixon>Pretoria.
Peter achoke ndi chitsilu kwambiri.