Email a copy of 'Chiukepo return boosts Malawi squad' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
KAMPAPALIKE
KAMPAPALIKE
8 years ago

3 kwa du!!!! Tiwone. Mwina nga mapuleya akunjawa atati alowemo. Zimatimvetsa chisoni kwabasi. Zomangoluzazi zizatha liti a Malalawi?

paul dowa
paul dowa
8 years ago

Even atabwera molinyo kudzakocha malawi mapuleya athu salimbikila vuto sikochi ayi makochi athu anapita kusukulu ndiye tisawanyoze ngati wina alipo apite akakoche iyeyo paka tidziwina osamapanga ndale mupira zopusa zimenezo paul dowa

zowanigeo@gmail.com
8 years ago

coach sikufuna uchoke koma selection yama player ikukuvuta chomwe chativulaza apa ukufuna zaiwe basi osati ife amalawi sichazeru kuti any game we loss kodi team inatenga ndalama pa joni inalibwino kwambiri koma iwe mtawari wampwasula wapanga yako nde kaya tiona zabwinozose pamasewero a lero

Toney Gondeh
Toney Gondeh
8 years ago

Kumalawi mpira kulibe tiyeni tivomere kma ufiti

James Mkoko
James Mkoko
8 years ago

Watikwana Ernest Mtawali azipita basi.

Uncle Ken
Uncle Ken
8 years ago

Ngakhale Chiukepo Akhalepo Flames Singawine 3 Kwa Du Zosatheka Doro Ndi Chipuwa

Mbiya Syangu
Mbiya Syangu
8 years ago

Mtawali akafunse Mponda .Makani za ziii.The is snr National Team not U’20.This time we will loose 3:0.

Manyazi.
Manyazi.
8 years ago

nkhani ndi coach sichina.

Blessings Kaweru
Blessings Kaweru
8 years ago

It can’t happen for the coach to leave out experienced players he got what he wanted

ankhoma
ankhoma
8 years ago

l knew mtawali as amare player not acoach so why assigning him with this big task? why not giving him asmall time like sure stream and see how it will progress rather than taking him to coach national team.guys we’re not serious. so dont blame him. kinnah.ngonamo.chimodzi maybe atleast.

Read previous post:
Thank you mothers music video by Mike Akiti: ‘Ndimathokoza’

After releasing the song “Ndimathokoza”, musician Mike Akitivi has put out visuals for the track and the music video is...

Close