Email a copy of 'Citizens protest against Admarc: Maize shortage in Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Citizens protest against Admarc: Maize shortage in Malawi' to a friend
Malawi High Commission in London has issued a warning those competing visa applications for the United Kingdom (UK) to be...
Mwaziona lero kuwawa ndi kupweteka zomwe mudakolola posakha DPP komaso Peter. Mai Joyce Banda sanatizuze ngati tiri pano.chakudya kusowa,ndalamaso ndiye kusoweratu.Kodi pamenepa wa cashgate ndindani?
Atsogoleri nakummwera mumabweretsa njala m’Malawi. Shupiti zanu.
John Kapito!…John Kapito! Where are you? Your maize consumming constituency is under attack! How long shall it take you…to to to lead us!
We need change tatopa Chimanaga tilibe, kwacha kuagwa, zinthu kwkwera daily, alibwino IMF endetse dziko
kugwa ndi jerwa yo ola. mkulukukulu. amaika njerwazo ndani. zitsiru za …. njerwa inayamba ya ola ku state house. chidina chimenecho chionanyowa.
Why was this not happening in Kamuzu’s time? One would just go to Admarc and buy a bag of maize at the price published. What system of government suit malawians especially those intrusted with the running of government, MPs, MINISTERS and PSs
Chakachino tiona bwadza, iliko njala, Petulo sizikumukhudza
Where is APM in all this mess? What action is he taking? He should be telling the minister in charge of ADMARC to hassle, and get his act together. Get the maize to the people, for crying out loud; they have the money, and they have to eat.
Akakudyereni ku chipatala eti? Kulibenso chokudya chili chonse uko.
ADMARC ikagwere uko. Asa.
Bola lilibe mphamvu loika mitengo Mr E Phiri. Devish Polapola Party yalephera basi. Petulo walephera
Azimayi anyengedwa ulele chaka chino sizidaonekenso. Pafunika kupezelatu thumba la gondolosi chifukwa ntchito yo kwata yiliko chaka chino.