Email a copy of 'Civil servants' salaries are delayed: Malawi govt says no cause for panic' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Civil servants' salaries are delayed: Malawi govt says no cause for panic' to a friend
Simon Itaye, the Managing Director of Packaging Industries Malawi, Nampak Limited has replaced Clement Chilingulo as chairman of the conglomerate Press...
Mulandiraso pa 15th after that they after that mucokocho ukubwera wa reforms pa August.
komabe bola, zaka zapitazi zimaonjeza, every month salary kucedwa, awa bola ndithu ngakhale zikundiwawa poti anandizoloweza kuti ikamati 24 ku health kuno zimakhala kuti zalowa
Tisadmdaaule alomwe ali mbwalo anthu wozikonda wopanda chikondi
Mbuye timenyeleni nkhondo
we were told that saulos chilima being someone from private sector will bring change to civil service, and the change you have brought is the delay in paying salaries to civil servants. Shame on you. What you promised to Malawians during campaign is a complete difference with what is on the ground.inu mukumwa tea wa mkaka.agalu omatililana pokwelana zitsilu
No salary palibe kupita kuntchito
They are willing to spend MK300 million for independence celebrations and they have no money for salaries???? what kind of maddness is this Komanso Mathanyula!
A cstu nawonso ali chete.mnanena za 21 days zija mpaka napano anthu akudikira yankho kapena what next eeee! koma pamalawi pano
Zanu zinalowa kale
Boma Limanamadi. Osawauza Anthuwa Chilungamo Kuti Kwavuta Ndi Ku Reserve Bank. Cheque Disbursement Apamapanga Ndi Munthu Mmozi, Ndie Munthuyo Wa…………….. Basi Zonse Zasokonekera. Akuopa Kuchita Manyazi A Boma. Nenani Basi Zachitika.