Lanjesi what shall they pay you? They are failing to pay other players there at BB iwe ndiye akakupatsa chiyani. Osapita kumeneko. Civo is a team of wise men stay put mwna iwe wamva??????
yuona
9 years ago
Good thinking John! Ku Bullets kapena ku Wanderers kuli ukapolo sizinaoneke. Ma player amawayendetsa wapansi akaluza komanso ku training amadya nzimbe kuli kushota. Wiana asakunamize mphwanga matumuwa amangowala kunjaku koma ali ndi mavuto adzaoneni,
Yankees
9 years ago
Lanjesi, Sunafikepo koma matimu aku Blantyre wo, amafuna kuti upite patali, tawaona Shoes pano ndi Mr announcer ku radio, Mponda ndiwachikulire ku Suresteam acadamy, Inuyo mukatha ku Civoko mudzapanga chani? Kapena ndinu a Skool ngati a Walter Nyamilandu? Kapena mukufuna mukamamalizika adzakulembeni Uphuzitsi wa primary skool? Mbuli ya Player ngati iwe zoona munthu ungakane ku Nyerere or ku Bulets kumalawi kuno? Ndiye pitani ku army teams chifukwa mungadzagulitse Somba ngati anzanu timawaona mu Chisapomu ena ndi aja akuyendetsa min Bus aja, kkkk! Shame!!
Why does bullets want this guy yet they have miracle gabeya.aren’t they aware that he’s defender of the moment.musamufookese mwana.
Angoni satha onse.
9 years ago
Lanjezi u r going to regreat.u wll end up zea.mark my words.
yes
9 years ago
BB ndi Wanderers, muzipezerera matimu enawo . ku Civo kuli ma official a sukulu!
elder sage2
9 years ago
‘Kintu’ is a mature player indeed. No rushings in these things. Dan Chitsulo got his exposure from right there at Civo. The chap akudya money ku Germany with a white wife to boot! A good player can get exposed from any team, even a military side as was the case with Dave Banda. Other Malawi very successful ‘feetball’ exports like Ernest Chirwali Mtawali, John Maduka, Stock Dandize, and Love Chafunya never played for Bullets nor nyerere Wanderers. Am not sure whether Limbikani Mzava, Robin Ngalande, Atusaye Nyondo – our current exports who also turn up for our national side –… Read more »
Wa Maule weni weni
9 years ago
BB is bigger than one “Lanjesi”. BB has gone through turbulent waters and rough roads and still managed to come out of all those. Our strength is not based on one player called Lanjesi or lalanje. BB thrives in the power of its supporters that’s why we are called the peoples’ team. Next time some wisdom will be pumped into your senses and regret that you did not come to BB. After all I sympathise with you malawian players for we all know that yours is short carrier. Make hay while the sun shines.
Uchindami
9 years ago
Timu yomwe ili ndi ndalama zokwanira imangopeleka ku timu komwe akufuna kugulako osewera zokambirana zikayenda bwino. Koma pomwe timu yofuna osewera igwiritsa ntchito bodza ponyengerera izo sitilora!
unzanziona lanjesi kakamila ku civo.