Email a copy of 'Civo not ready to sale captain Zoya -Mtelera' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Civo not ready to sale captain Zoya -Mtelera' to a friend
Malawi's acoustic kings Edgar and Davis will headline the first eviction show of the 2015 E-Wallet talent competition slated for...
You CIVO management be realistic, government is failing to employ nurses & doctors ndiye Zoya mukamulemba muzimupatsa chani? This is total lie, how many players for CIVO which are employed by government? I have neighbours who are playing for CIVO but struggling with no job in government, musiyeni mwana akaone zina ku Nyasa Bullets timu yolemera kwambiri pa Malawi pano, kale mumati timu yopanda sponsor, pano munganene kuti chani, leave Zoya to decide what to do? Afterall everyone has got his style of life akaona nazo zochita ndalama azikalandira ku Nyasazo. Fisher has done alot with football ali ku BB… Read more »
Whose captive is he going to be once sold?
kma zya nd wabwno
Government has no money at the moment. Can not employ people. Do not tell these players lies.
Boma lakanika kulemba ntchito ma nurse ndiye ndibodza loonekeratu kumanamiza maplayer acivo kuti muwalemba ntchito,iwe Emmanuel Zoya bwera ku NYASA BULLETS chi team chokhacho cholemera kwambiri mdziko muno komanso chodziwa kudoda mpira.
I will love Big Bullets forever.
Mpira umakoma ndintchito ainse, khala komko akupatseso ntchito kaya njaukalaliki kaya floor manager bola ntchito
Zoya adanena kale kuti season ikubwerayi atumikira bullets nde enanu ndi nsanje yanuyo mukhaula zeni zeni
Welcome zoya ife manyasa bullets amfana ofewa kwambri chimtumba chilipo kkkkkkkkkkk or titha kugula civo yonse ukunva bwanji pamenepo?????
Employ him that’s the only solution to stopping him from leaving