Email a copy of 'Commissioner of Lands offices stinking over unpaid water bills, workers down tools' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Commissioner of Lands offices stinking over unpaid water bills, workers down tools' to a friend
Is Malawi becoming a useless nation or are Malawians becoming a useless lot? Imagine how ‘maizegate’ has stopped everything and...
Koma Mtumbuka uyu Kwame Ngwira wapanira maplot….akungopereka kwa Nyirenda, Munthali, Mwenifumbo, Gondwe, Msowoya, Msiska etc. Zoona zimenezo
Ku Lands ntchito ndi kuba basi. Pano ndiye a ku Lands anyanya zogulitsa idle plots zoti eni eke ali kutali. People buying plots please watch out. Most plots looking vacant have owners. Vuto ndiloti mabwana ndi amene akutsogolera zaumbavazi. ACB afufuzeni a china Ngwira, a Lands Commissioner ndi gulu lawo, akuba too much, kugawa malo mwachinyengo too much.
mma ofesi ambili mulibe proper facitities za toilet. zitsulo zina anakonyola konyola iwe ukalowa ngati mlendo mose wayamba kuzungulilila kusowa poponda pogwejemulila, nanji tissue forget it ena apititsa kunyumba. iwe kudabwa kuti abwana amatani mmimba mukafunda? nanji klina amakayangala kutiko?????????????? nde bola kukumba zimbudzitu.
umaonabe kuti a mw fe nde tilibe ukhondo. bwanji pa ma airport pathu, eish nyasi zakezo, unimmaginable. anyway pa cileka after 51 yrs amanga lounge yanyowani zimbuzi zake za ma see through glass mochingilamu,nde bola munakaitana ma chinese atimangile zooneka ngakhale zimakhala zosakhwima kwenikweni nchito za manj ao.kkkkkkkkk
pa mw panotu ndi mmene zimakhalila. mma ofesimu muli taasikana, taanyamata tamake dzana tima top bosses ta Form 2. ana aoo thooo. ana azicemwali ankolo niephews agogo ao kuwaika pa gate. koma ena akati afuse ncito ma paper ali nao amauzidwa kuti ma paper ao ngosakwanila yet azibale ao alibe ndi ya 8 yomwe
mmmm following
what happens to the funding you get this is poor management of resources
Koma Lands in poorly manages its clients and even itself. Shame on you. Muleke providing false hope and dehumanizing staff
Koma chi boma cha DPP chilibe ma priorities. mxiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
GO TO STATE HOUSE !!!!
These are the results of handpicking managers for some of the important Government Departments. They do not know how to prioritize expenditure (of lean funding). This big office is managed by a PO grade officer while some senior officers are around for the very same reason of manipulating him in all land related issues including allocation of plots. The Regional Office is run by remote control from their head office at Zowe House. No wonder corruption will not stop at this office. Big fishes at Zowe use this Regional Commissioner of Lands (PO) as a figure head to transact their… Read more »
Mawu, @Makonyola, there is too much politics in this office. The Regional Head is just a figure head, the Pon behind the whole game of land/plot allocation. No wonder the guys are filthy rich and amassed themselves and their realtives with lots of plots. Its time this office gets a reshuffle.