Email a copy of 'Coach Chimodzi welcomes Malawi ‘fair’ Afcon draw with caution' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

33 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
godfrey
godfrey
9 years ago

Zilibwino bola osazatichitisa manyazi manena nokha kuti its fair draw

mchongolo kwauma
mchongolo kwauma
9 years ago

yambani pompano kukonzekera koma SAILESI OSAMUSIYA mwana waluso kwambiri

Kanyasyo
Kanyasyo
9 years ago

Guinea is good, if we lose to Guinea that could not be bad,Koma whale mpaka tizaluze ndi ku Namibia and ZIM.Zim inali kale.AFAM tulusani ndalama zopangira ma preparation mwachangu because failing to prepare is prepararing to fail.

angoni
angoni
9 years ago

Adzatisosola. Our players can’t handle success that is why we lose crucial qualifying games. Mbatama.

matako m'mwamba
matako m'mwamba
9 years ago

I can see Malawi qualifying for afcon and I don’t doubt about that.

Paul Samudeni
9 years ago

chifunika ndikukonzekera bwino komanso posankha ma player osasankhira maina kapena mbiri koma luso limene ali nawo panthawi ino

Chimangenimapiko
Chimangenimapiko
9 years ago

We trust you You. Those who say Kinah was better ,how come he is struggling in SA. You are a better coach coal not big headed like Kinah. We will support you.

Chiko Baluwa
Chiko Baluwa
9 years ago

Tigazidwanso tidazolowera a malawi.

yabwata
yabwata
9 years ago

Fair group zaboza young umakhomelera kinna uziona azakuswa ndi ma boys ako

Santa
9 years ago

A Young kukondera basi busy kutenga Ku camp mwana wanu ndi anthu omwe mumacheza nawo. Mpira sungapite patali choncho

Read previous post:
Lutepo exonerated in Mphwiyo’s attempted murder: ‘ No evidence linking him’

Lead investigator in the ongoing Paul Mphwiyo’s murder case, Kankwala Chilinda has revealed that there is currently no evidence linking...

Close