Email a copy of 'Controversy surrounds North Malawi League, fears of match fixing' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Controversy surrounds North Malawi League, fears of match fixing' to a friend
Malawi national football team, the Flames will be seeded from the preliminary round of the 2015 Cosafa Cup due to...
Northerners,every season wararawarara eeish.Mpira simutha ntchito kugawa mapoints mu super league basi m’malo moti muzilimbikira kumpoto kukhale matimu olo 4 mu TNM ntchito kukokana eee federation eee Nyikaland.Nanga kupanda Moyale kumalimbikira bwino kulibe team kumpototu
Why is it that our colleagues from the Northern League fail to be demonstrate professionalism? If your failing to manage a small league like Simama, how about taking the leadership? Muzazitha inu? Your collegues from the Chipiku nad Nsenjere have identified the promoted team kom ainuu year in and out mlandu basi..Utumbuka eti
Palibe kugwirizana pakati pa mpira ndi federation.Mukungosonyeza umbuli wanu abale inu.Sukulu ndiyofunika.Federation izachitika,mufune or musafune,Mbuzi Inu
even in parliament akumamenya anthu ogwira ntchito ,nkhanza too much how can they rule since they have shown the world their disorganisation in simple things & they can not be trusted with bigger things
Always Mzuni is on loosing side though amakhala ndi valid reason
Koma Kumeneko North Woyee!
atumbuka! Eish!
Still, Federation is the only answer. Then we can have our good sons who are at FAM come home and help run things.
Kodi zantchito mwaiwala mwasanduka a mpira? Tikhale ndi matimu angati mu super league? Bwanji ndalama zimapita ku mpirazo mutakonzetsera manyumba akukhalira kuukhawa. Two or three military teams ndizomwe tikufuna osati mpaka akwane six aaaaaayi zikumatichititsa manyazi. RSADF munaimvapo mu ABSA league? NRFAL sakulakwisa nawo zawakwana. Nanu a FAM chitaniponi kanthu mwa nsanga super league isanasanduke MDF league
Koma kumeneko ku nyikaland. Nanga mukazakhala panokha ndiye eshiii zizakhalakotu.
Anthuwa ndi mbuzi zenizeni,samadziwa kuyendetsa mpira achoke.