Email a copy of 'Court convicts truck driver over matola' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

6 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Malawi Citizen
Malawi Citizen
6 years ago

Apolisi ku Lilongwe pa boma pao pa M1-PMF, traffic light madzulo alionse masiku antchito amaonelera anthu amakwera ma truck kulowa mseu wa Mnchesi, Kawale ndi Area 23 iwo akukupiza magalimoto ndikumaona ndi maso zonse zochitika. Nthawi zina amakhala 20 meters away kuchokera pa junction po mumseu wolowera ku Mchesi and lore ikadzadza amalandira zam’manja pompo-pompo. Chilungamo tsono chilikuti choti wina pano aziti convicted pa nkhani ya matola. Anangokana iyeyu kupereka za m’manja zija zimafunsidwa kuti mukwanitsa zingati kodi? Kodi ichi nchiyani a Malawi? Tikupita kuti pa liwiro limeneri? Blame game siitithandiza koma kulongosora zinthu moyenerera. Sober mind is needed. Putting… Read more »

chatonda Mvula
chatonda Mvula
6 years ago

This is very silly. Please release the driver. Some roads in Malawi have no minibuses operating. How will people travel in rural areas of Malawi now? Please, let the government be aware of the realities on the ground and never punish people for their poverty. You will need them during elections too.

gaga
gaga
6 years ago

When are closing Tyre Bank. This chinese company is selling used tyres that is a big risk to many.

Azowa
Azowa
6 years ago

Uku ndikupusa kumene kukuchitakaku.Dziko la Malawi lotsogoleredwa ndi anthu ophunzira koma mbuli za anthu.Amalandira ndalama zingati ameneyo munamufusa,licence ikatha amamukhomera ndindani?Musanaweruze ziganiza kaye.53 years of independent koma anthu anakali muukapolo osasimbika.Mulungu akukuonani ana anjoka inu.

superheroes
superheroes
6 years ago

an offence endangering their lives??????? anawakweza ndani mu track? i thought anakwera okha. Malawiiiiiiiii.

Kandawe
Kandawe
6 years ago

Nkhani ya MATOLA yomweyi mpaka kumangana ngati wanyamula chamba, mmmm guys chosechoso anthuwo athandizidwa kuyenda ulendo wawo,eeish my Malawi

Read previous post:
Maneb fires MSCE invigilators

Examination administrators, the Malawi National Examination Board (Maneb) has cut the number of invigilators for the ongoing Malawi School Certificate...

Close