Email a copy of 'Court dismisses judicial review on UTM registration: Lawyer Bob Chimkango ‘frivolous’ application thrown out' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

38 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Zayang'ana ku ngolo
Zayang'ana ku ngolo
5 years ago

This is abuse of court process allow the registration of UTM and do not block it. We are in multiparty democracy but DPP want to take us aback. APM was not there when we were voting for this democracy and please don’t spoil.

Bakha
Bakha
5 years ago

Even DPP itself is flavorous, vexatious and hopeless. Anthu osamva!

pathfinder
pathfinder
5 years ago
Reply to  Bakha

Komatu abale azizi akupanga si a DPP koma a MCP. Mundikhulupilire ndithu, umboni ndiri nawo. Team MCP siimafuniratu UTM ati chifukwa ndi team b ya DPP komanso ipatula ena mwa mavoti a MCP. Musade DPP siikutekeseka ndi bus company, amene akubvulala kwambiri ndi a MCP.

Chicken
Chicken
5 years ago

Retard lawyer now appointed Company Secretary. This Bob has failed miserably to run his own firm and boot licks DPP kuti awonekeko pa town otherwise he is a fucking useless citizen. Hule lachabechabe

Tsogolo langa
Tsogolo langa
5 years ago

koma ndiye mwalimbana naye uja mumati babe………….UTM/SKC moto kuti buuuuuuu 2019 boma

Game Changer
Game Changer
5 years ago

…….’frivolous, vexatious and hopeless’….. koma apumbwa muli ndi khama osangozitaya bwanji

goodwellbanda
goodwellbanda
5 years ago

Musamalimbane naye chilima mukuva kuwawa

Gwamula
Gwamula
5 years ago

Well written brief news item there Wongani Chiuta. Many out there do not accurately report court proceedings.

Kanyimbi
Kanyimbi
5 years ago

A Mike Tembwe kumaiona game ngati ma lawyer onse m’Malawi muno akungolozera kwa UTM musamaletu ndi MCP yanuyo a Chakwera chiyambireni campaign anadzangodutsa ku Zalewa mpaka ku Mwanza & reverse osaoloka Shire waku LL via lakeshore road ndiye kudziwa campaign kumeneko, anthu ali mu BT koma a Chakwera kumangolambalala eeish!

Uladi Kenneth
5 years ago

Mcp kkkkkkk vuto la a Malawi sitichedwa kuiwala

BigMan
BigMan
5 years ago

How can anyone fully grown person vote for DPP?

pathfinder
pathfinder
5 years ago
Reply to  BigMan

Simply because he is a grown man. Ana onse aku mkaka, osakhwima pamchombo, obvala thewera apite akavotere mwana nzawo khanda baby chilima. Omatenga anthu azipani zina kumawapatsa ndalama kumawalankhulitsa pamisonkhano yake nkumati ajowina. Ndichifukwa chake anthuwo akumayankhula poyera kuti abwera kudzagwira ntchito ya malawi congress party pa msonkhano wachilima.

Read previous post:
Bushiri’s book launch dominates media in Southern Africa 

Key media houses in Southern Africa continue to be awash with extensive coverage of Prophet Shepherd Bushiri’s launch of his...

Close