Email a copy of 'Court grants lawyer bail: Mulemba involved in K50m Malawi cashgate' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Court grants lawyer bail: Mulemba involved in K50m Malawi cashgate' to a friend
In a bid to motivate and inspire academic excellence in young people, Airtel Malawi has pumped K2 million towards secondary...
Tsiku anaomberedwa mphwiyo akulu awa sanagone kusamutsa ‘akatundu’ kunyumba kwa mphwiyo…otiuza kukhala mkazi wawo…ndipo on that day they met mphwiyo at Lounge Onthambi, nde amene mukuti mkulu ndiofatsa mungokamba ma style akabedwe and washing the money thru Knight & Knight amapanga ndiyeyu…azathu aku FDH Bank anatiuza kale kuti account ya Knight kumalowa ndalana zodabwitsa zedi…lets wait & see!
Mulungu oweruza aweruze basi…anthu oyipa inu osauka kumafa mzipatala inu mukudya kashi ya boma muli pheee…yakwana nthawi musova!
Head spinning! The hunters have been hunted mphakana khola.
Yambani siwakuba chabwino, ndi wa money laundering! “For now”
Yambani kaya si wakuba kaya chani, koma na apa anaba. Chomwe amati khikhikhi ndi mphwiyo nchani, amadziwa kuti adyapo. Amalandila zingati to acquire all these properties within 5 years isaa. Mukumuyikila kumbyoni ndi amene mukamupempha amakugayilani,
Joe and Max lawyers also facilitated the same for the owner of the Matindi. Money was from Lutepo to Mserembo through the law firm. He bough a mansion kwa Bvumbwe. Are you ACB going to arrest the lawyers too?
Head of crooks is Ralph Kasambara. Lawyers are struggling these days.
Amangidwe basi anthu akuba amenewa
LET JUSTICE PREVAIL
Maloya ndi mkangowaona akudusa but now am getting the real picture!