Email a copy of 'CSO’s link electricity crisis to Malawi failed leadership: Call for 'Day of Rage'' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'CSO’s link electricity crisis to Malawi failed leadership: Call for 'Day of Rage'' to a friend
High Court judge Charles Mkandawire has rebuked the Anti-Corruption Bureau (ACB) for “not being serious” on matters of national interest...
Nzodziwikiratu kuti DPP yawononga Malawi. ESCOM ndi company ya boma a dpp amapita ku ESCOM kukatenga ndalama za campaign ngati momwe anachitira ndi Mzuzu city council and LWB and BT city council. Wina afune asafune boma MCP ikutenga come 2019. Tifuna anthu ofunira Malawi zabwino osati alomwe odzikonda okha. Anthu tikukhala mumdima wa ndiweyani a dpp akuti chimenecho ndiye chitukuko, cry my beloved country.
CSO’s in Malawi is but helpless and clueless believe me NO sensible Malawian can listen nor follow you now. You are like a crocodile without jaws – you like eating donors money by cheating them that you are fighting for the voiceless but when you recieve money you call people to the streets who are usually killed or wounded afterwards you escape to your mansions safely leaving the poor in cold blood.
Iiii komanso azibambo ma gay inu mukumatibowa tsopano. Mulibe chochita china? Nthawi yolimatu ino anthu azipita pa nsewu azikapanga chani? Tikakayenda magetsi abwera?? Kodi mukalemba ma proposal anu then kulandira ndalama kwa ma donor mumatiitana kuti tikapange march tikagawane dollar zo. Fotseki
olo iwe wa DPP kunyumba kwako kulibe magetsi lero
escom should employ foreign experts or privatise it, if it stays under government it is always prone to financial abuse and things will never improve
Iwe cloud ndi mphaso kodi amakutumani . ndindani? mkwuziwa nokha kuti ntchito za magetsi ziri Manja mwa Escom chochulirapo DPP ndichani ofunika kukufufuzani mmene mumakhonzera muli pa secondary level chifukwa zimene mumachita zimaonekeratu kuti osayamikira DPP angakhale kamodzi kokha munthu amathawa pa njingay mubvekere DPP aaa Muyalukanazo
Olo chitsiru sichingayamikile DPP ndiye iwe nyaxy ukudabwitsa kuti mwina umadya mabi mutu wako suyenda
Nyaxy ndiwe munthu opusa kwambiri, kuwombera mmanja mfiti za DPP bwanji? Escom is totally under government if u don’t know, and panopa akutizunza, kupha, mabizinesi athu aima, tikusowa pogwira and you talk rubbish!!! A stupid fool, kapena umalemba utamwa midoli or you smoke whatever weed?
These people are misguided, they are forgetting that this problem emanated due to lack of proper planning by our previous governments, if ever they have solutions why not engage government and share their suggestions? ?? I think we have a lot of people who are mentally unwell in this country.