Email a copy of 'CSOs yet to drop demand for Mutharika resignation' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
iwe
iwe
8 years ago

unamva kuti aku india kuli chitukuko wayenda kangati kuti akukatenga chitukuko antcheya abingu a joyce nawoso amatero zopusa zokhazokha kumalawiko kulibe munthu olamulira wa chilungamo sadzapezeka basi anali kamuzu basi zina zonse panja pangali pangali

P chakwana
P chakwana
8 years ago

Ma bungwe simumalifunila dziko zabwino mmalo mopeza njira zoti ziko lithane ndi mavuto mumabwezela ziko pansi always you talk shit kuti zinthu zizinkelabe kusonekela mumatelonso nthawi ya bingu njala pomwe mvula imavumba mowononga bwanji simumayilesa munali kuti? Mukalandila mafunding anuwo osapeza zochita zina bwanji ? Nonse ndi zisilu

kazionere njowenjowe
8 years ago

They are few people who are rich because they are working. Sometimes they become rich because they steal money from the organisation they are working or they take some allowances from mere staffs who sent for a workshop. In Malawi nobody can become rich without doing something evil like kuponderezana, kuzilembera ma allowance ambiri, katangale, kugula katundu mokwera mosiyana ndi mtengo weniweni ndizina zonyansa zimene zimapangitsa kuti dzikoli lisatukuke. Ine chimene ndikudziwa ndi chakuti program imene yayambidwa ya community technical colleges ipasidwe ndalama zambiri kuti itheke ndipo ipitilire. Ndi imodzi mwa ntchito yomwe ingapangitse kukweza chuma cha dzikoli lino. I… Read more »

Sailota
Sailota
8 years ago

Mukumva kukoma imvani, koma musatiletse ife kulira. May God intervene in any way He sees it good to most Malawians. I did not choose to be a Malawian; God chose it and I believe He is not happy to see me crying! Amen.

ochenji
ochenji
8 years ago

CSO’s hv weak minds they thought that economy can just change overnight, I know them has received money 4 foreign countries. Iwo akutumidwa ndi otsutsa tikukuonanitu. APM woyee!

Muhiphethere
8 years ago

Mapwisi genu inu a CSOs. Confusionists you are. One day, we shall grab you CSOs by the neck coz mwaonjeza. Fwetseki!

Aubrey Norman
Aubrey Norman
8 years ago

Mwasowa zoyankhula mupite Mayiko anzanu mukawone momwe anthu akuvutikira,Ikakhala Njala ndimvula yomwe inawononga mudazolowera kupempha basi malomoti muzidalire panokha,mukukana misonkho mwayiwara kuti ndalama zake zimagula mankhwala zipatala?mukuti Economy yavuta mwayiwala kuti mukukana kuti muzipanga Mathanyula?Ndiye amabungwe opeleka zithandizo adakwiya osati amabungwe ake aku Malawitu ayi athuwa koma kupempha ndi kuba.Mukanati muzikhala ndikumayiwona Dziko momwe ikuyendera munakadziwa kuti zinthuzo sizikuchitika Ku Malawi kokha,Gwirani ntchito molimbika mulungu adzakupatsani.Mulungu amutsogolere Peter Wa Mutharika pa wulendo wake wa ku India komwe akukatitengeranso Chitukuko china.

kennzo
kennzo
8 years ago

Now we can see these cso’s are rubbish like peter. who’s going to protect us and tax payers money hehhhh?
who are we going to trust if cso leaders plainly showing us that the received bribery from ministers to crusfy poor malawians.
Our hearts are burning one day you will suffer the worst, God help we need your help.

kumangoni
kumangoni
8 years ago

Waphwisa Kanyimbi,mbewa zonse kuti bvuuuu

America
8 years ago

The next election poor people will never vote cso is them who is going to vote (dogs)

Read previous post:
FIFA new resolutions bar 4th term: Blow for Nyamilandu’s FA Malawi power extension

A good leader is one who knows when to leave office as is a good visitor knows that a good...

Close