Email a copy of 'Daniel Mulomo drags MCP to court over polls' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Daniel Mulomo drags MCP to court over polls' to a friend
Electricity Supply Commission of Malawi ( ESCOM) shunned a kalondolondo interface electricity assessment meeting leaving different stakeholders furious and warned...
Ngati analephera ndikuzivotera yekha. Not worthy. Just sit down and accept the results. Old fashioned man. The only thing mr mlomo can do is to become a shadow khansala for 2019 elections. Munalepheretsa chipani. Asiyeni amzanu abweretse mzeru zina. MCP for new blood
Had it been apezako timavote tochepa koma olo,ayi zisiyeni zakukhotizo kkkk.
Umodzi, Kumvera, Kukhulupirika ndi Kusunga mwambo should talk to Mulomo as earlier as possible.
Why did he participate in the illegal pools? If he won , would he have sued. The challenge with the old guys is they always think of their posts as zamuyaya.
A Mlomo adalowa nawo mu mpikisanowu ndipo analuza ngakhale ndi voti imodzi osaipeza, ngati chisankho chidali chosayenela adaloweranji, ndipo palibe amene adawavotera ngakhale mmodzi out of 400 voters?, koma mkuluyu adaipitsitsatu, kodi atabweranso anthu ovotawo poti ndiwomwewo adzawavotera, mwaulemu angozisiya izi nthawi yawo adyerera ndi mnyamata wao uyu kamata amapangira limodzi madilu azisankho kusiya anthu anthu kumatemga mphwemphwa atagawira ndalama zotsatira zake mzimenezi, Kamata paja adamthamangitsa kale pampano wa Director of Elections – kapumeni bwino malume
Mulomo ukuyankhula ku khoti kkkkk.
Ndichisankho Chanu Chomwenso Mwaberana Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk Atambala Akujomphana.Heeeeeee Koma Nyenwa!
The works of DPP
How was he ambushed when the party announced about the polls through a press conference 1 month b4 the polls.What is unconstitutional about the polls when the MCP constitution stipulates that the tenure of office bearers is 3 years and yet Mlomo held this position for 7 years.The Dude is just confused that he is out of mpando wonona (posters chipani ndi ma shadow).He is finished!
Alomo vetsetsani ndimene dziko limayendera inu osapanga protest mukhala ngaa muwukira