Mhuu,last time twas The Messenger,now its Davido. Ku Nyasaland kumeneko.
kenman
9 years ago
we knew davido wudnt b coming to malawi…
Grant C
9 years ago
Malawi kukhumudwisa,,mmalo momapeza ana amene aphukila kumene pa music,kukayimba ndi davido mukutenga nkhalamba,,ife brackmissionalys,,lucius banda tinatopa nawo,,kodi nanga gwamba,dan lu,,mwanache,,grant C,majako,john T,,ndi ena achichepele ali kuti???,,plz promote young stars not magogo like soja,and missonaries,,tinatopa nawo
Gondwa
9 years ago
I knew this show was not going to work. Ife we have been UDF since time immemorial and very skilled for that matter. We have contributed immensely to the party. We understand Malawi’s media and entertainment industry and you know that. Yet you chose to work with this guy who failed in Kenya and you call him your strategist? Fine your strategist but what does he know about organizing shows? The moment i met this guy going to promote this show at a Christian radio station in Lilongwe is when i knew he doesn’t know what he is doing and… Read more »
wobeba wanga
9 years ago
Well done.
Straight talk
9 years ago
Abale kodi za Davido Concert zikugwilizana chani ndi Atupele. leave my President alone. Ndi dhilu and mukudana naye chifukwa he is principled. He is the only one who can save this nation from the economic turmoil we are in. Lets leave our personal problems and not politicise everything. UDF why do you want to reap where you did not sow? Just save yourselves from further embarassments and put your hse in order. why wash dirty linen in the public? anthu opanda nzeru inu.
KENZO mataya
9 years ago
Wawatu wawa,muthu uyu sizaboza ,ndangwilakonaye ntchito,simuthu oyamika olo pangono.stop ndithu sawerengera kuti wathandizako chani.chihana adatani,ulendotu inu umeneu. Mwana amaliladi nditulo lake lomwe.basi basi ungono ungono ulendo. Ngati akukanika ka go green nde ziko anakalitha.?chiwaya moto moto
Abiti Mtila
9 years ago
Ine ndinanena kuti uyu ndi baby. Chipani for sale.. koma chatha ngati makatani
wayellow weniweni
9 years ago
Koma kumupanga chipongwe Lucious zoona? ndiye ndi zoonadi kuti achina Jamieson, Josh, Fawzia Osman, Adam, Ngwira, ANdanga anaponya paliponse. abale Ndanga ali mbuuu kikikikii koma amandimvetsa chisoni mwamva. Or running mate mmmhhh sakununkha kanthu. Koma Lucious yekhayo ndiye samutha akunama. Chimene chija ndi chitsulo chanjanji. Soldier ndi survivor. ife tidzavotela Lucious ku convention ngati president lol
nothing new here,…he cant come ofcoz….