Email a copy of 'Death of NRC student: Court convicts Malawi Police officer, acquits 2 cops' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

25 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
God is Good
8 years ago

Ndangogwira pakamwa ine, Dziko la Malawi lopanda Ntendere.

apundi says
apundi says
8 years ago

nanga mumati ku south africa nkhaza, nanga uku ndi ku south africa, shame on police

Khonsolo
Khonsolo
8 years ago

Bad news

gladstone kaka
gladstone kaka
8 years ago

This is what happens when you employ dull policemen.Interrogation means intimidation to them.Who were working during the shift when this guy was ruthlessly beaten by these dullards?Do you know its common in Malawi working while drunk on cheap sachets and some even high on weed while using police vehicles.Are police supposed to be using police vehicles in drinking premises during working hours?

TSAKHO LIMENELO
TSAKHO LIMENELO
8 years ago

This is what is happening when STATE police abusing power to Malawian citizens and on other hand STATE police are violating SUPREME LAW which is CONSTITUTION

Uzionela iwe ndithu you will be jailed brother after 21 days

CHAONA MZAKO CHAPITA BWANAWE chatsala KWA IWE wa police bad move

ADA VUWA
8 years ago

zonse zimachitika kusowa chikondi amalawi tiyeni tikondane monga nationality yanthu tikuziwikila chimavesa chisoni apolice omweso ali mbali ya boma kumapanga zinthu zankhaza nanga anthu apanga bwanji mukubwelesa mavuto ndinu ndima nyakanyaka anuo nyokonyoko

makwinjaishmael
makwinjaishmael
8 years ago

I wonder why we dont have such brutal acts from MDF koma apolice. Last year munapha msitikali kuzomba. Boma lamalawi limakuikilani kumsana kwambiri, koma one day mudzasiya,mudzayamba kugwira ntchito zanu moyenelera.
Mulungu azikukhululukirani,

Apao Kugola
Apao Kugola
8 years ago

Indeed, apolisi ndi zitsiru. The problem is that the Government recruits officers into the noble profession those who are intellectually deficient, stupid and imbeciles. Even if it was following the adage that says: If you want to catch a thief send a thief, ku Malawi kuno zanyanyira. Ndiye tikalemba pano kuti a polisi mukuwonjeza misbehaving wina adzindiwopsyeza ndikakumana naye. Some of us were born to call a spade by its name.

Anayenera kumangidwa wonse.

The Fearless Samurai (Jwampiriu)- Wa Kongeresi.

ndadabwa
8 years ago

apolisi athu ndi agalu. zomwe amadziwa ndi rape ndi murder. kutereku akonzeka kuti amuphe Joyce Banda akamabwera next week

Mphwere
Mphwere
8 years ago

Simumati police yasintha nanga pali kusintha apa?

Read previous post:
‘i want to die,’ says Malawi man aged 113

A defaced black Rhodesian metal identity card states his date of birth as June 6, 1902, meaning he has officially...

Close