E-Mail 'Dedza Young Soccer coach Pofera resigns' To A Friend

Email a copy of 'Dedza Young Soccer coach Pofera resigns' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
newest oldest most voted
Notify of
de' Morgan
Guest

He is back!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Kanyimbi
Guest
Kanyimbi

Pakafa nyama agalu amachuluka.

Blessings Marenso
Guest
Blessings Marenso

Pofera Knows The Truth

Yankho
Guest
Yankho

Jegwee osadandaula bola iwe watenga Dedza Young Soccer to another level. Uli ndi zambiri zoti uchite mwina anthu sakudziwa bwino. Ngati ma Officials anayamba kuyerekedwa ataye tiye tilimbikire kuyendetsa chipani chanthu cha Malawi Congress party ndi nzeru zakozo MCP 2019 boma. Za mpira zitaye uko, taona timu ya ku Drdza ikuyendetsedwa ndi Atumbuka iwo akufuna Federal System koma ife sitilora team ndi ya Dedza. Nanga a Temboawauuza kuti iwe akuchotsa. Panopa a Tembo ndi wokwiya kwambiri ndi zimenezi. Team slogan yake ndi Kwacha ndipo tonse amene tiri ma Supporter ndife a Kwacha. Ndamva kuti a Tembo atuma President wathu wokendeka… Read more »

Name*mkuzi ulimba ndimbina
Guest

Umbombo mwawona ngati mulemera nazo.

namalira
Guest
namalira

panganeni ndiwe osokoneza galu iwe sikwanutu kumeneko and jegwe pa easy agawe ma points amenewa basi mukuwona ngati ma gate collections muzidya angati muli ndi ma supporter ku bt inu akapamba well done coach.

BALITCHI baliman
Guest
BALITCHI baliman

Osadanda Jegwe, zinayamba ndi John Chilembwe izii.

Simeon Nyapala
Guest

Papa wangozolowera kutukwana basi umati asasiye ? Ndi ufulu wake u HSA sintchito?

BALITCHI baliman CHIMPEPA
Guest

mumutaya lero jegweyo?? poti wakuchotsan mmatope. plz my home district team dont do that.

Munyapa pakhwili
Guest

Andrew bonya kaya mumati bunya wakondwano eti?sapesa zitsitsi ukuona ngati super league ndi chipiku eti?tiyenazoni