Email a copy of 'DePeCo invades Kasungu with message of hope, thousands of people attend rally' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DePeCo invades Kasungu with message of hope, thousands of people attend rally' to a friend
Malawi police from Area 30 headquarters in Lilongwe have arrested the northern region immigration chief over immigrants syndicate. Police are...
Koma wosakomo zimene mukuwonazo sizinayambe zenizeni muziwona tizipani tizipani tanu tosawukato kudalira ndalama zamunthu monzi mulira Chaka chake ndichino MCP nkachaniso.
The mighty party 2019 Dr.Chris Daza Boma viva DEPECO viva Dr Chris Daza viva wina alira akuwona ngati anthu akusapota zipani chifukwa cha agogo awo pano anthu anazindikira MCP ndi DPP sizipaniso za agogo DEPECO chachinyamata sitikufunaso nkhalamba.
Bambo Daza kodi mwayimitsako ma councillors ku Milonde ndi ku Malindi kapena ka chipani kanu kakadali mu chikwama , mukamati democratic people’s congress mwati basi kachipani kameneka kalowa mmalo mwa MCP, zosatheka muwafunse a Nthanda Congress party (NCP) kuti anathela kuti akuwuzani. Ife takonzeka kutulutsa DPP m’boma ndi Chakwera. Anthu enanu dyera, munathawa ku MCP chifukwa sanakusankheni pa upulezidenti wa chipani ku convention. Muzingolubwalubwa choncho basi!
It makes some people feel happy when they see a group of people in front of them showering praises………so keep on dreaming sir and enjoy life.
MALAWI NEEDS REVOLUTION !
MALAWI NEEDS EVANGALISATION !
MALAWI NEEDS COMPLETE OVERHAUL
MALAWI NEEDS NEW LEADERS
MALAWI NEEDS YOUNG VIBRANT
LEADERS
BUSHIRI IS THE MAN OF OUR
GENERATION !!
ADaza akudyerani anyamata ndi atsikana a mu KU
Yayi ku kasungu ni kwa tambara wa kuda imwe namwe.Akungo kugwirani mmaso chaje.