Email a copy of 'Discorium to host Morgan Heritage after party' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Discorium to host Morgan Heritage after party' to a friend
Two students have committed suicide on different places and different reasons in Dedza. Dedza police spokesperson Edward Kabango confirmed. “It’s...
Amwene olo atangoyima kutsogolo osayimba ife tipitabe kukawona. zanu ino!!
Ozitsatafe tipita koma iweyo sumazitsata khala choncho. Morgan Heritage – Royal family moto kuti buuuu
Mr. Major General, if you don’t have money to burn just shut up. Many singers today don’t use live bands. Ine olo atabwera twenty times, I will still go and enjoy the show. Tikakhala enafe it’s not the quality of the music in these shows that matters but the socializing aspect of such shows. Long Live Morgan Heritage!
Koma a Malawi mm ayi ndife opusa kwa mbirit.zomwe anachita anthu wa tayiwala azingo tidyera ndalama apa.tiyeni tipange sponsor oyimba athu.ine amenewa nde ayi sindiza pitako ndipo sindikugwilizana nazo zoti abwele kuno
ANTHUWA ATIONERERA POTI NDIFE MAZOBA A MALAWIFE NDIZIMENE ANACHITA ZIJA ZA MA FLASH IFE BASI KUKOMEDWABE KUKANAKHALA KWINA SAKANAYESANSO NDIKUBWELAKONSO KOMWE