Email a copy of 'DPP's Ben Phiri says UTM presence only on Facebook: Most of its social media users are abroad, not voters' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

76 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Prophet
Prophet
5 years ago

Take it or leave it

MCP analamulira 31years
Pano a kwanisa 25 years ali ku opposition(Muluzu 10yrs,Bingu & Joyce10yrs and Peter5yrs)
Zakhalazaka 5yrs ndi 1 yr kuti a balatse ekwezyoni
Sopano kuti a balance ekwezyoni ayenela kuti this year a luzetso kaya mwadala or mwamwayi

Akaza balance ekwezyoniyo tizawavotela

Mussa
Mussa
5 years ago

UTM rocks!! kkkkkkkkk

Iantana
Iantana
5 years ago

So we should take UTM seriuosly eti? out of all opposition parties why single it out? palinkhani apa

sato
sato
5 years ago

The DPP gurus know they will face stiff competition from UTM and may lose so Ben Phiri wants to project UTM as an outsider and in so doing deflect its potential. I have interacted with supporters of DPP and many seems to have a soft spot for MCP which says a lot about the chaos in DPP following the rise of UTM.

Patrick Mbewe
Patrick Mbewe
5 years ago

Mulungu akafuna kusintha ufumu , zonse amapanga yekha kuti ulemerero onse ubwere Kwa iye. Werengani bukhu la Daniel , muzaona nokha . DPP ikuzichosa yokha, akukhala ngati misala. Nkhani yavma alubino, kopereka nomination papers zonse zosokonekera.
Zina ndi izi. Mmalo Moti tikhala tikukamba za mfundo zomwe anatsitsa kuti mchifukwa ninji DPP isankhidwenso, mutu waukulu pa interview ndi Oti he is denying the force that is UTM when all Malawi knows very well.
Ambuye tikudziwa kuti DPP mwaichosa ndinu. Tingodikira mutiululire president wina pa 21 May.

Wiseman
Wiseman
5 years ago

And most of them are leaving outside malawi, they can not even come and vote. Akugwira ya kalavula gaga ku south africa, kuyenda mozemba everyday. ku USA, England. Enawanso ndalama ya transport kuti abwere kumudzi alibe.

Jumani Jumani
Jumani Jumani
5 years ago
Reply to  Wiseman

Kaya izo ndi zanu. Ife ndiye tikuchinda azungu, amwenye, ma Filipino, aluya , ma Brazil mkati inu zichedwani nkutinyoza

JJ Mbewe the Pathfinder
JJ Mbewe the Pathfinder
5 years ago
Reply to  Jumani Jumani

kkkkkkkkk koma iwe jumani, wachibwana eti?

Wiseman
Wiseman
5 years ago
Reply to  Jumani Jumani

Ndiye ndizonyadila zimenezo, za ziii!!!!. Kumangopanga noise pa social media. Mumkaona ngati mukapita kunja mukapeza money mosavuta, lero ndi zimenezo or 100 usd, 500 Rand mulibe yoti mungawatumizile makolo kumudzi.

Wiseman
Wiseman
5 years ago
Reply to  Jumani Jumani

Za ziiii, mukatero kubweleko muthatha kuno, kudzavutitsa achibale ndi kugula coffin chonsecho la mchele simutumizako

Thinktank
5 years ago
Reply to  Wiseman

Za ziii…….just check misonkhano ya chilima….it’s nonsensical to say it’s only supported on social platforms.MCP DPP are also on social platforms defending there respective parties……..

Getu Maseko
Getu Maseko
5 years ago

DPP kuba, kupha and kuononga. Abale athu a chi Albino akusowa mtendere in their own country. Ben Phiri ndiye mbava inanso. Iwe ndi Nankhumwa mwagwira chipwisi. Mumaona ngati mudzalamula dziko lino. Mbuzi inu.

Wokonderedwa
Wokonderedwa
5 years ago

Aphiri akunama awa, nanga iwo akweza chibagela bwanji kkkk, UTM yakuzunguzani mpaka mwaiwala kuika chala mmwamba mwaika chibagela kkkk

REGISTERED VOTER
REGISTERED VOTER
5 years ago

That can be true…but still be very very carefull with MCP….because MCP is only adding day in day out…But DPP has subtracted a lot…as DPP we have subtracted the lower shire , Ntheu, and UTM is bring confusion in Lomwe belt areas..
So be carefully with MCP….

Khima
Khima
5 years ago

1 DPP
2 MCP
3UTM
4UDF

The margins will be in minority though.

Aman
Aman
5 years ago
Reply to  Khima

Only that you don’t know …just wait and see..
MCP is winning these elections mark my words

JJ Mbewe the Pathfinder
JJ Mbewe the Pathfinder
5 years ago
Reply to  Aman

Eeeh paja mmawina choncho ndi pakamwa, nthawi yakeyo ikadzakwana muzidzalira kuti mwaberedwa kkkkkk koma MCP simunaphunzilepobe chilichonse?

Nganga solibala
Nganga solibala
5 years ago

Ben wabandulidwa , kkkkkkkkkk ,
Apa akumva pheeeeeeeni ndi UTM

Read previous post:
Zeeya Creations calls for support of youth owned businesses

Founder of Lilongwe based multimedia company, Zeeya Creations, Albert Kamanga has called upon the private sector, government and all the...

Close