Email a copy of 'DPP candidate survive disqualification scare in Mzuzu' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

10 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Concerned Citi
Concerned Citi
8 years ago

Koma a DPP ndinudi atonga eti Ndi suit yoyiyamikila imeneyo and uhundsum uli pati apo, m’malo muyakhula za chitukuko busy kulemba useless apa. Candidate wanu mufuse zomwe anapanga kwa Luwinga or just go ku Chibavi police akakuwuzani, in brief his wife anamenyana ndi chibwezi ku Luwinga market, komaso ali ndi mwana ndi mkazi wina ku Chiputula This shows uhule samubayaso ndi masipoko ameneyu Chenjelani amalawi povota komaso inu a kazi anu amayenda ndi iye take care

Chibanja tv
Chibanja tv
8 years ago

Just look how handsome is the DPP candidate! lol a very expensive suit uyutu akukwana nanga zinazi kolala ya malaya onyenyeka nyenyekawo. Enawo ndiye olo kuvala jacket koma ziliko.

Chipalamandule
Chipalamandule
8 years ago

Amake Wize Mafunde supporter eeeeshiiiii!

Chipalamandule
Chipalamandule
8 years ago

DPP yiwalani koma Aford ndi mcp.

Pacharo
Pacharo
8 years ago

Kodi kani?

Omega
Omega
8 years ago

Pakana PP candidate , manyazi alibe , chipani choti mtsogoleri wake ananyamuka kale , wokabisala , ma Vice President onse anazitaya , running mate wake wazitaya , sing’anga wawo Mayi Chiponda amangobibidwa tsiku lonse kusowa mtengo wogwira ,kuteleko chipako chamudyelela Mdyomba Ibrahim Matola ndi mdyomba mzake Ralph Jooma , pamodzi ndi amtchona aja amu National News Paper a Ken Msonda .Potsiliza aulutsi mundipelekere moni kwa midyomba ya PP iyi , Che Bayisikolo , Che Kalamka , Che Matigadi , Che Sipindulo , Che Sadulo, osaiwala Che Foloko , pamodzi ndi ambwenumbwenu onse moni moni moni .Potsiliza a mkozi mundisweweleleko nyimbo… Read more »

zachepa
8 years ago

why so many candidates for the ward.

Keen Observer
8 years ago

Nyirenda no wonder you’re a stringer indeed you’re not a journalist, is this a story worth reporting???? Even Nyasatimes you’re losing the Mojo, the problem of being biased.

fisi
fisi
8 years ago

you headlined the story as of dpp at the end u say its not only dpp and others went to the extent of disqualified. what cld be the head line here? you are oiling the candidate

madalitso
madalitso
8 years ago

ada u r now dpp??? thats good my old friend at chibavi primary school together with emmmanual zgambo, tawinani tiwone ndithu

Read previous post:
Catholic church underscores importance for Malawi to invest in children learning centres

The Director for Pontifical Missionaries Society at the Episcopal Conference of Malawi, Fr. Vincent Mwakhwawa has described Early Childhood Centres...

Close