E-Mail 'DPP fight with Prophet Bushiri goes ugly:  Cadets sing anti-Bushiri songs at Chinga funeral' To A Friend

Email a copy of 'DPP fight with Prophet Bushiri goes ugly:  Cadets sing anti-Bushiri songs at Chinga funeral' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
newest oldest most voted
Notify of
Jackson Kathumba@gmail.Com
Guest

Major 1 God Bless You, Pitilizani Ntchito Yabwino Yomwe Mukugwila,posatengela Zomwe Akuyakhula Anthu, Kodi A President Bwanji Mukhalangati Mwana Wakhanda? Mudzikula, Major 1 Simungamfike Or Mutadzola Mamina Amunthu Wamisala Aaraa.

mahomwa Nyika Republic
Guest
mahomwa Nyika Republic

Bushiri the Nyika Republic Billionaire the richest man in Nyasaland history God bless you keep own helping poor malawians they are not DPP children’s but God never punish people bcz of stupid leader we have todays God will fight for you.

Evangelist Enganados Mbewe
Guest
Evangelist Enganados Mbewe

Anthu otumikila mulungu, gwilani ntchito osayang’ana nkhope, ndi nthawi ya ana a Yehova, tinakusiyilani dzikoli kuti mwina zinthu ziyenda komanso mwakanika

Ambuje apali
Guest

Signs of the times

janet phiri
Guest
janet phiri

shame on you . kuzolowera kulemba macoomment otukwana basi. ndiye choncho mululungu asakwiye anthu amulungu ndi osapemphera onse kumangolakhula zofanana. lord have mercy on us

emmanuel chikuse
Guest

kodi bushili amalakwa chani? osafooka bushili go deeper

2 options
Guest
2 options

Guys
Chuma sitigawa ngati madzi. Even madzi amene timatha kugula. We should be very careful tikafuna kumusata munthu Chifukwa cha zinthu zomwe alinazo.
Tisayiwalw ndale za pamalawi sizikhala ndi nthawi.
Timayiwala kuti campaign anadusa pano ndi nthawi yokonza mavuto aziko lathu

Upulofeti anthu ayesa ngati business especially akangonena and zinthuzo nkutheka mmmmmmm nde kuti atiputa timachita kukagonera komweko kusata zozizwa ei

Petre Mathanyula
Guest

You think by disrupting funeral service then you’ll automatically win the 2019 elections. Kunali anzanu a UDF ankapanga zomwezi ali kuti lero, Mulungu simunthu, You’ll regret this. Watch this space.

Umziya
Guest
Umziya

Even if he stands for president ndiye vuto ndi chani. Agalu a DPP mumaona ngati amalawi mulipo nokha eti.

John Kapala
Guest
John Kapala

In my whole life I have never seen a SHAMEFUL Political Party as DPP.