Email a copy of 'DPP flat out to dislodge two Mzimba female MPs Nyalonje, Chiluba' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

18 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
hatton
hatton
6 years ago

A Chakwera alankhula kudzera mwa Kusamba Dzonzi kuti ku Mpoto kuli anthu ochepa chonco sangataye nthawi ndikuchita chitukuko ku mpotoko. Komanso a Chakwera anenesa kuti anthu a kumpoto samawafuna potaya Msowoya ndikutola Mia. Its up to you people from the north to choose the party that specialized in butchering your sons. Rememder how MCP disrespected Yatuta’s body at Queen Elizabeth Central Hospital mortuary when MCP officials addressed their members while standing on Yatuta’s dead body. Remember what MCP did to Dunduzu. Remember how MCP killed Orton Chirwa, the father and founder of the MCP party. Amenewa ndi anthu ovoteredwa ndi… Read more »

Arwe
Arwe
6 years ago
Reply to  hatton

We also remember how DPP butchered the 21 innocent people in Mzuzu

Kenny
Kenny
6 years ago

A Biniwelo inu. Okula vumbwe otantha patsekela .inu nkumajijilika mwayesa ka mcp kangatenge boma? Tamangovinani gule masiku adzipita. Chakwera adakanika kutenga2 boma kwa mzimayi Joyce Banda nde mwayesa kwa achalume APM angayesele?
Chonde mudzakhale patali ndi temiki pa 21 May pano.

Sauzande
Sauzande
6 years ago

Mwati munthuyi ndi mkazi or mwamuna ? Koma ku mphoto koka ,ine ayi ” CANT NEVER “

santana
santana
6 years ago

@ Do you know that DPP got Parliamentary seats in the north while it was in opposition? What does that teach you? An empty tin makes a lot of noise. When will you people open your eyes? The party which has been torturing you for decades is the one you are fighting for yet you have been crying for 31 years that MCP was bad. May be MCP knew that people like Odala are just to blind to notice good from bad. To such people the torture is part of their life. The MCP is saying it flatly that if… Read more »

Binnwell Kachikopa
6 years ago
Reply to  santana

Iwe santana kay satana! You are very way back of current political waves, dont think you evil dpp will stay forever! Cashgate unadya iwe inakupanga twist ubungo wako. Your dull professor is very old and forgets everything in a due course so we cant waste our time with such ordinary rusty brain and your cawardice should be near to death because for sure you are headless with your walking devil dpp

Kenny
Kenny
6 years ago

Mphatso
U mean whete was MCP in those 31years ?Did the bridges have to wait for APM in only 4 years? Think again

Odala
Odala
6 years ago

Ndalama zakuba zathu kumapangila kampeni. foseki. Kumpoto kube zanu. 10% yanu kuopa kulira

Mphatso
Mphatso
6 years ago

This behaviour yomangoti a state president alamula kuti ma bridge awiri amangidwe must come to a stop.chiri chinse a state preside.kodi APM amakhala kumenekoko?inuyo ntchito yanu ndi chiyani?nchifukwa chake zinthu zikalakwika anthu amyamba kutukwana nazo president.za ziiiii

Kenny
Kenny
6 years ago

MCP game yawakulila.Asowa pogwira. Inu mungafunse kuti 4 years anzanu a DPP anali kuti? Mesa inu munakhala 31years kulephera kumanga mabridge omwewo? Ife tudikila mabilijwo ndipo 2019 Peter Mtharika timupatsa voti yakathithi. Osafuna akakolope nyanja.
Paja mwati mabridge asamangidwe kumpoto chifukwa kuli anthu ochepa? MCP siizasinthadi.Tithana nanu chaka chake ndichino

Binnwell Kachikopa
6 years ago
Reply to  Kenny

Dpp ndi MCP game yakulira ndani akulu inu opanda nzerunu! Muli pa Malawi pompano koma! Mumva mkodzo simunati! MCP MORE FIRE!

Kenny
Kenny
6 years ago

Gong’ontha

LEGO
6 years ago

That’s total rubbish how can you promise to build bridges because of the elections?Where have you been all this time to embark on these useless campaigns?Shame on you DDP!

Read previous post:
Tchetha and Chiotcha to exchange punches on March 4

Boxing fans will flock to M1 Centre Point in Lilongwe on March 4 next month to witness a fierce non...

Close