Email a copy of 'DPP justifies political violence against MCP at Chilembwe memorial:  ‘We’re ruling Malawi’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

19 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
UMODZI NDI MPHAMVU
UMODZI NDI MPHAMVU
7 years ago

LETS AWAIT 2019

santana
santana
7 years ago

Kodi 2019 kulidi chisankho? Nanga opposition sikupeza munthu weniweni wodzapikisana ndi APM bwanji? Wasting time commenting on Nyasa instead of going in the field to meet voters. Munamuona bwanji Nankhumwa kogawa zinthu kuja? Ngakhale msonkhano wa Chakwera ku CR ungafike pamene paja? DPP ikutenganso bomali 2019 because opposition ndi mbola zokhazokha.

Chazovu
Chazovu
7 years ago

what shows here is just primitive politics there is no territory for any party , every part is free to go anywhere we are in a Multiparty system of Government this total no sense and not accepted DPP must stop this with e mediate effect

Alinafe phiri
Alinafe phiri
7 years ago

Munthu zitamukanika amathamangira kuopyseza azake,Atakhala President wanzeru akuyenera kudzudzula makhalidwe oyipawa komaso zomwe alakhula a Kasaira zukutsimikizira kuti DPP ili ndi anthu opanda nzeru okhaokha amene mbongo mwawo muli mamina okhaokha.Kodi aliyese atati azipanga zimenezo ndiye kuti kukhala nkhondotu chifukwa a MCP nawo Ali ndi Madera awo.

lisitoni wawononga
7 years ago

Dzikoli ndi lathu dzikoli ndi lathu koma pitalayu wawononga afe afe pitalayu wawononga
dzikoli ndi lathu dzikoli ndi lathu koma mtchona uyu wawononga afe afe mtchona uyu wawononga

Binnwell Kachikopa
7 years ago

Dpp is a walking devil that must be erased from Malawi, its leaders and most supporters are educated salvages good at stealing and killing, they are devils puppets who clad in devils regalia full of ignorance. There secretary general Francis Mphepo and their party leader are idiots who don’t know what life entails, they are cowards who din’t learn a lesson from their mose walero death. Let them know cardiac arrest redeemed us from Bingus brutality and this time the same cardiac arrest will redeem us from this dull professor and your stupid Kasairas who always back up on every… Read more »

namalira
7 years ago

Komansoo awa akuti a mmc ndinu wotani,or manyazi mulibe??why do you always talk zopusa against MCP..???be civilized babaaa..try to be human sometimes,mmmxiieww.

Daniel
7 years ago

Oh, but I remember during campaign Kanyoza a DPP cadet was driving a car with flash light on APM’S convoy , that time they were not beaten though they were lving in denial that Bingu was no longer the president.
Chakwera has never done that.

Fabiano Kamanga
Fabiano Kamanga
7 years ago

IF IT WAS A CHURCH FUNCTION, WHY ISIT THAT DPP SUPPORTERS WERE PUTTING IN PARTY UNIFORMS. YAMBANI MWACHOTSA CHISOSO M’MASO MWANU MUSANAYAMBE KUKANGANA NDI ENA.

INU KU CENTRAL REGION SIMUMAPITAKO? KUPUSA!!!

Mccarthy
7 years ago

Mulungu akufuna kuti Mutseguke Maso amalawi, Don’t ever do the same mistake in 2019. Malawi suppose be a milk & honey right nw!!!!

Read previous post:
Journalists Union of Malawi slams govt’s invisible political machinations to muzzle media

The Journalists Union of Malawi (JUMA) has slammed some "invisible political machinations" behind the action  by the Malawi Revenue Authority...

Close