Email a copy of 'DPP not shaken with breakaway UTM: Jeffrey says ‘victory is ours 2019’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP not shaken with breakaway UTM: Jeffrey says ‘victory is ours 2019’' to a friend
Malawian tax authorities on Wednesday stormed privately-owned Zodiak Broadcasting Station (ZBS) in Lilongwe and asked one of the country's biggest media firm...
Nangozo has a beautiful smile, she is really a beauty! Achiswe kakumbeni dzenje mudzikwilire, anzanu akuona zomwe mwasankha kuti musaone ndi khungu lanulo mukhalira kutsutsa boma mpaka kalekale.
U think so.
Kwavuta nanga a Mussa alowakuti tsopano, Kaya zanu izo
Does this lady live on planet earth? She clearly does not live in Malawi if she thinks the President and the DPP have successfully run the country for the past four years.
Patricia Nangozo uyu watsatira mamunake VP wa eastern region. Mmalo mokapanga campain muli busy kuzigulitsa pa nyasatimes? Akudoda Yunus Mussa uona!!
Kodi a nyasatimes wakupatsani zingati Nangozoyu? Tikhalira iyeyu? Mayi Nangozo Ng’oma yoliralira sichedwa kung’ambikatu, ohooo. Musambulidwapo apa
Kuba inu, simungawine . Deal ndi Chakwera basi.
haha koma mayi awaaa aaaah kumasiyako mau kuti mawa muzapeze zoyankhula
Ana achepa – akayamwe kwa mayi ujha.
Koma chitukuko chokhacho mzozodo Peter Mutharika and his government akuchichita zochita kuoneka ndi maso.