Email a copy of 'DPP, rights activists condemn Chief Lundu’s ‘reckless’ attack on Prophet Bushiri church' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

24 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
vuyisile ntombayithethi

olo kuwona majekete akewo, umangodziwilatu kuti ndiwodwala mutu wawukulu!!!!

cliff
cliff
6 years ago

Chief cool down

Piko
Piko
6 years ago

Kkkkkkk a stupid person and a party can distance itself but we all know where that stupid rally was organised by dpp so dont put yourself away from lundu……who gave lundu the podium? Mwasowa pogwira abale akakhala madala akutukwana kkkkkkkķkk…..akuti stupid critics…..

mathews malata
6 years ago

Lundu ndi munthu mmodzi amene amagwiritsidwa ntchito ndi chipani cholamula cha DPP, kumbukilani pamalilo ena ake ndiyemweyu emwe ananyoza chakwela koma boma linakhala losangalala kwambili ndi zolankhula zake ngakhale panali pamalilo,lelo ndizimenezi wayamba kunyozana ndi amipingo– samala iwe lundu ndi chipani chakocho, ulibe udindo omuweluza munthu kapena mpingo ntchito imeneyo umusiile amene anakulenga iweyo…Zopusa basi

Joe Gibson Mandimba
Joe Gibson Mandimba
6 years ago

Mfiti yaikulu iyi…Kukonda kunyenga tiwana..
Mapazi ache!
Tamuoneni nkhope yacheyo!!!

Rodney Bamusi
Rodney Bamusi
6 years ago

Komatu mfumuyi kuletsa kupemphera yapala, koma nonse mukudziwa kuti kikunena zoona….. Munthu uyu siwa Mulungu… Mkuluyu akulowa ndale ndi Chris Daza,, mkuluyu ndiwa sataniki zoona…

sick man
sick man
6 years ago

Forgive him. He is a sick man. His utterances are under the influence of drugs.

Generations of vipers
Generations of vipers
6 years ago

Mfumu ikamalankhula mbwelera chonchi, dziwani kuti imfa yake ili pafupi

charombanthu
charombanthu
6 years ago

Why is this so called chief given the podium to utter such careless and reckless remarks? He is usually under the influence of alcohol obviously. Chiefs are supposed to be unifying characters and not dividing people this way. It is very comforting that the ruling DPP has distanced itself from such careless remarks. I am not a Bushiri fan or follower but surely this utterance from this chief is nonsense. Someone must stop giving him the podium, for heaven’s sake!

mwana mchwewa
mwana mchwewa
6 years ago

kenaka timva kuti azipani zinazi musadzachititse msonkhano ku dera langa kkkkk mafumu amasiku ano amenewo ukuona ngati DPP ikupatsa kenakake walemba mmadzi

Read previous post:
Malawi President hire two new High Court judges: N’riva and Ligowe

Malawi President Peter Mutharika has appointed two new High Court judges. High Court of Malawi and Malawi Supreme Court of...

Close