Email a copy of 'DPP’s Mchacha in fierce verbal tirade against Chakwera, JB and Chilima' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'DPP’s Mchacha in fierce verbal tirade against Chakwera, JB and Chilima' to a friend
Vice President Saulos Chilima drove all the way from Dowa to Ntcheu late Saturday afternoon to condole families who lost...
Mchacha umanveka ndi nkhani zoipa mdziko muno. Violence komaso umbanda…. if Mcp come to power you and ben phiri… mudzakalowa ndende .
There are case’s waiting for you. If speak against your opponent monyoza its up to you. You have the right but pray hard. Because MCP government, shall track you down.. uli ndi mbili zoipa za chinsinsi
analipo winaso ku BT nthawi ya MULUZI anafa ngati galu uja. amalallata heavy pa misonkhano.anthu tikati kucoka mmamizi mwathu kuyesa tikamva za nzelu, anta time wasted, enerrgy and njala kungotipalaso mmimba ,mvula naitikantha, iwo ali ofu ofu kutithawa mmagalimoto a ndalama ama taxes athu.(KAPITO)
Mwnw akatoimapa culu uja sha.
nde awabolakoakanalowezapa ntima STUDENT COMPANION yokha. koma mutu okhala ngati ciboli wu ,ah ndakaika sakanaitha
Savage weniweni ndiweyo Nchacha. Munthawa after 21 May Malawi muno. Lidzafika tsiku udzatha ngati makatani. Udziwe Mulungu iwe udakali ndi moyo.
It was monitored on Mchacha Broad Casting ( MBC)
Truth hurts. Mchacha has said the truth
Koma ndiye mwamulalatiratu. Wagona ameneyi kkkkkkkkk. Akulalata maliseche a DPP ali pomwepo. Mukhaula agalu inu, mwasala ndi one month salary.
Uneducated fool makes alot of noise
He had blessings from APM to say what he said.
The man is desperate. However, he was right to say somebody is receiving salaries without working. That’s bad
mbuli iyi inu